Khasala amenyedwa ndi achitetezo a boma ku Nsanje
Achitetezo akunyumba ya boma amenya khansala wachipani cha United Democratic Front (UDF) m'dela la Ruo m'boma la Nsanje, Mariko Mulotali. Izi zinachitika kum'mawaku pomwe khansalayu anamvedwa akunyoza utsogoleri wachipani cha Malawi Congress (MCP) nthawi yomwe… ...