Ku Malawi kwabadwa chipani china Cha PDP
Mtsongoleri wazipani zotsutsa boma kunyumba yamalamulo yemwenso ndi phungu wanyumba yamalamulo wa dera lapakati m'boma la Mulanje Kondwani Nankhumwa walengeza kuti wayambitsa chipani chake cha People's Development Party (PDP). A Nankhumwa, womwe anachotsedwa mu chipani… ...