
La fote limakwanabe, Bambo ku Kasungu anjatidwa atabvulidwa chigoba
Bambo wa zaka 23, ali m’chitokosi cha apolisi m’boma la Kasungu pomwe akuyembekezeleka kuyankha mlandu ofuna kuba mu dzina la polisi. Bamboyu yemwe dzina lake ndi Lonjezo Banda, wagwidwa usiku wa lachinayi akufuna kulanda njinga… ...