Anthu 7 apezeka ndi kachirombo ka Covid-19 ku Nsanje
Pomwe anthu ochuluka anayamba kuiwala za matenda a Covid-19, zadziwika kuti matendawa anakalipo mdziko muno pomwe ku Nsanje akuti anthu asanu ndi awiri (7), apezeka ndi kachirombo koyambitsa matendawa. Izi ndi malingana ndi a George… ...