Anthu aulesi ndi omwe akutukwana Chakwera – watelo ‘prophet’ Habakkuk
…wafusa kuti kudzala sidi kwa mneneri ndikukapeleka kwa “mahule” chabwino nchiyani? Mneneri otchuka m’dziko muno, Habakkuk yemwe sanakhalepo pa banja koma akuti wachita zigololo kwambiri ndipo pano akudikira nthawi ya Mulungu kuti akwatile, wati sakuona… ...