Mpira wa kuno ndi mbwelera, angosewela ngati ndado – watelo RVG ponena za Supa Ligi
Amene mumagundika kupita ku ma bwalo kumapeto kwa sabata kukaonela mipira ya Ligi ati mwina pena mumakangoonela ndado basi chifukwa mipira ina yakuno ndi yosalongosoka. Pena mwina ukuonela utha kumayesa anthu angosewela ndi ndodo. Malingana… ...