
Arsenal yathetsa ulendo wa Real Madrid oteteza UCL
Kunali chimwemwe usiku onse ku timu ya Arsenal, pomwe yasosolanso michonya, akatswiri kangapo a Real Madrid pa kwawo Santiago Bernabeu mu mzinda wa Madrid usiku wa Lachitatu 2-1 mu masewelo achibweleza a ndime ya ma… ...