Tinali akapolo, ndagwililidwa ndi amuna angapo β amayi aulura nkhaza za ku Oman
Amayi omwe adali mdziko la Oman komwe anapita atanamizidwa kuti adzikapatsidwa malipilo ochuluka, achenjeza atsikana ena kuti asamakhumbileko ponena kuti ku dzikoli kuli ukapolo osasimbika, ndipo wina waulura kuti wakhala akugwililidwa ndi bwana komaso anzake… ...