Nyumba ya boma yachotsa wothilira maluwa pomuganizira kuti amaulura zinsinsi
Mayi yemwe amagwira ntchito yosamala maluwa a Tiyanjane Mlangeni, omwe akuganizilidwa kuti ndiosasunga pakamwa ndipo akhala akuwulura zinsinsi zochuluka zokhudza kumpanda, inde ku nyumba ya boma, achotsedwa ntchito. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe boma… ...