Ntchito 1 miliyoni pa chaka? Haha ndi bodza la nkhukuniza – Mutharika
Wandisokosela n’kulinga utamva, ndipo chulukechuluke ngwa njuchi yomwe umanena iwe ndi yomwe yakuluma. Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika wati zomwe akunena wachiwiri wawo a Saulos Chilima zoti pasanathe chaka azakhala atapanga ntchito 1… ...