Anthu akhungu la chi alubino ati miyoyo yawo ili pachiwopsezo pomwe chisankho chikuyandikira
Anthu a wulumali wa khungu la chi alubino ati miyoyo yawo ili pachiwopsezo ndipo ali ndi mantha pomwe chisankho chosankha mtsogoleri wadziko, aphungu akunyumba yamalamulo komanso makhansala chatsala pang'ono kuti chichitike m'dziko muno. Wapampando wa… ...