
Zathapo: Achotsedwa sukulu kamba ka utambwali m’mayeso
Sukulu ya Ukachenjede ya Malawi yachotsa ophunzira makumi awiri (20) kamba kochita zachinyengo m'mayeso. Malinga ndi chikalata chomwe tsamba lino laona, ophunzirawa, omwe ndi a ma pulogilamu osiyanasiyana pasukulupa, anachita kusaweruzika pomwe amaonera, kukopera komanso… ...