A PP ndiwo adachotsa a Chilima pa udindo
Boma la Malawi lati likudziwa kuti anthu otsatila Mayi Joyce Banda ndiwo adalemba kalata yoti a Saulos Chilima atula pansi udindo. Malinga ndi mneneri wa boma, a Nicolas Dausi, amene analinso mkulu wa u kazitape… ...