DPP will win 2019 elections – Dausi

619

The ruling Democratic Progressive Party (DPP)  has said  Malawians must not be cheated by the by-election results since DPP will win the mega elections in 2019.

Information Minister Nicholas Dausi said this to the  media in Blantyre where Malawi Electoral Comission announced results of October 17 by-elections which have seen the DPP losing to Malawi Congress Party (MCP).

Sidik Mia

Dausi: We will win in the 2019 elections.

In his remarks, Dausi who is a senior member of the ruling party said  the elections will help them to come up with new plans that will be vibrant to make it during the 2019 tripartite elections.

According to Dausi, it is not about how many times someone has fallen but it is about how much someone  realises that he has fallen and move forward meaning that the October 17 by-elections will prepare the DPP for the future.

Official results of October 17 by-elections revealed that in all three constituencies where the by-elections took place  namely Lilongwe Msozi North, Lilongwe South East and Nsanje Lalanje,  Malawi main opposition MCP  candidates  won.

In Lilongwe City South East Constituency,  MCP’s Ulemu Msungama emerged winner with 6,722 votes while DPP’s Reuben Ngwenya managed 3,597 votes.

Independent Candidates Christopher Joseph Manja and Ellen Shabani got 891 votes and 311 votes respectively.

In Lilongwe Msozi North constituency, MCP’s Sosten Gwengwe was officially declared winner  with 10,015 votes while his main challenger Bruno Daga of DPP  scooped 2,559.

The opposition MCP also beat the DPP in Nsanje Lalanje where MCP candidate Lawrence Sitolo was declared new Member of Parliament for the constituency.

In wards,  DPP claimed one ward namely Mayani in Dedza while main opposition MCP  claimed two wards namely Mtsiriza and Ndirande wards.

Share.

619 Comments

 1. mufunse ma mp anu or misonkhano sapangisa ku limbe tiri ndi noel masangwi mpaka pano anthu sakumudziwa kuwina kulipo mukomze zoofooka zanu ma mp ena akuononga chipanau

 2. One needs to be confident when embarking on any competetion. What Bwana Dausi has done is to express his positive feelings, which is his right; and such right could be anyone else’s as well. His projection may be the reality or not, come 2019 elections. What is required is for contenders to work extra hard if they have to achieve their desired goals.

 3. No more Dpp 2019, ngakhale a Dausi akunamiza anthu kuti adzapambana, mavuto achipani chimenechi anyanyira kuipa ndipo akungoyankhula modzilimbitsa mtima poti achita kale manyazi

 4. zikuoneka kt a Malawi umbuli wayamba kuchepa wovetera munthu Kamba kamtundu , chigawo, chipani pano anthu ayamba kuvotera munthu amene angasithe zinthu.Dausi akumpusisa peter mwalo mokonza zinthu ayenera kudziwa oponya voti ndi a Malawi

 5. Dausi keep on getting those funds which ur getting, but don’t wakeup and speak on behalf of my fellow malawians. That election must teach u enough mind you, accept the defeat and think of what next. My advise is that Malawians are no more sleeping as we knew what is good and what is not good stay away with your bomberstics English as Malawians said enough is enough get ready 2019 will be the same.

 6. Apa malawi walowa chisawawa azasauka mpakakare coz kusintha sintha zipani kumapangisa zikokusauka ngakhale mcp italowa muzapezanso zofooka muzati ichoke molomwake mbuli muzakhala inumumavota ngakhala kuno ku RSA kuno amayasesa kut chipani chaboma chisamasinthe thas why kulikolemera chikwa choti chuma chimakhazikika

 7. MALOTO ACHUMBA OMALOTA KUT UKUBELEKA KOMA MMAWA UNKUONA KUT WANYELA MNYUMBA IFE AMALAWI TATOPA NANU NDIE ICHI NDICHIAMBI 2019 AMALAWI ADZAVOTELA CHIPAN CHOMWE CHIGAPANGE NJILA YOTHETSELA MAVUTO AWO KOMA INU DPP GAT ADAUS NDI ABALE AWO ANGAWINITSE DPP TIDZAKUONAN

 8. MALOTO ACHUMBA OMALOTA KUT UKUBELEKA KOMA MMAWA UNKUONA KUT WANYELA MNYUMBA IFE AMALAWI TATOPA NANU NDIE ICHI NDICHIAMBI 2019 AMALAWI ADZAVOTELA CHIPAN CHOMWE CHIGAPANGE NJILA YOTHETSELA MAVUTO AWO KOMA INU DPP GAT ADAUS NDI ABALE AWO ANGAWINITSE DPP TIDZAKUONAN

 9. simoni petulo ndikukuuza lero lino kuti asanalire tambala wakuda amalawi adzakukana katatu ,,, bwana kumbukani padzana a malawi anakukanani mutangofika kumene ankati siinu m’malawi mpaka munalorera kuluza green card, lero ndi izi amalawi akananso through by~ election ,dikilani 2019 amalawi adzakukanani kachitatu ,,

 10. Kkkkkk Dausi ! Ndiwandaledi! Olo matenda kuchipatala ukudziwa kuti munthuyu afa! Timamuuza muchira Ambuye alipo! Koma tukudziwa kuti chabwino palibe! A Dausi ine ndi Prophet Mbeya , nwatsala ndi miyezi 18 kuchoka m’boma kwanu kwatha! Mwachoka Pataki kuyambira multi ku MYP mpaka piano mwadyerera muzipita kwanu kwatha!

 11. Remove anthu owumila campaign materials then DPP will win 2019 definitely, let me remind DPP boses, ovota ambiri ndiosawuka so make sure kuti candidate azidziwika bwino ndi anthu asawukawo.

 12. Aaaa koma the way DPP has done its campaign during this last by-election, I don’t think kuwina is there come 2019. To get a piece of Chitenje from campaign team iiiiiiiiiii

 13. Komwe mmadalirako mkumene athu lero akupopedwa magazi kma boma lanu la Dpp simukuchitapo kathu .olo kupusako athu amaboma amenewa azakuvotelani? Zokolora za alimi kuzigula mokupa chomchi? Angaku voteleni athu? Ndalama kusowa kumapezeka thumba laboma basi osati mtumba mwawathu? Adausi mumu uze peter alimbe athu achenuka.apange mapulani ena obela chisakho kma kupanda kutero ng’ombe zizayang’ana kungolo. Anthu boma la peter sakulifuna ngakhale pangono.Mcp inyamula boma 2019 keep this words sure.

 14. Daus akungofuna kumudyela Pro Peter, Bwanji osavomeleza ,A President avomeleza inu mutichani APA. Basi bwana Daus MCP door is open for you before it too late

 15. Wamitsala dausi iye sangawone kuti malawi wachangamuka tsopano ngati anga bele 2019 koma anthu achangamuka ndi kuwanamidza zinthu zika zikwela inu ndalama mmanthumba mwanu bweeeee 2019 vote ikupita ku new mcp kwaaachaaaaa!!!! Dausi ndindaniso mapadzi ake

 16. I think Mr President will never see people like mr Dausi still serving as minister because instead of kupita kukadya khonde ndikuona chomwe chapangisa kuti mugwe mpaka 5-1 muli buzy kubwebwetabe kuti muwina Malawi wake uti?…..This is a new Malawi Mr Dausi people are voting for aChange not zitukuko zapa MBC

 17. Mr.Dausi,ingomalizani mansion mukumanga ku mwanza,otherwise you won’t finish it after 2019 because you’ll be out of this corrupt government.

 18. Kodi anthuwa amasankhira chipani kapena ntchito za munthuyo? Apa zangoonetsa kut #DPP sinali ndi ma candidate abwino. Osati anthu amasala #DPP ayi, muwona kusintha ku mbali zonse za zipanizi ma primary akayambika, nde poti pano akupanga kapena kuti kuwonekera ku zitukuko ndi ma Councillor, chipwirikiti chichitika ku zipani zonse.

 19. If Chakwera wants to win must go back to church not politics how can a person ran away from God’s work tell him will end up like his uncle Zenus

 20. People who love udf as a party r now behind mcp because what the leader of udf has done is an embarassment to the party members,we dont love udf as a family but as purely a party and since we hv been left in suspence then we hv just joined the mcp to uproot this mess

 21. Chonde ambuye kumwambako timveleni ife akapolo anuu chilichonse mumachita ndipo mumampatsa umfumu amene mwamufuna tichotselen amutharika pau president akuzuza anthu anuu muiken okonda anthu osat mbabvazi

 22. Amalawi tiyeni tipemphe Mulungu kuti atisegule maso tikhale ndi presdent ovela anthu.Nanga Amalawi munavapo kuti Presdent agona ndi njala? Timavutika ndife chifukwa chaumbuli tiyeni amalawi tisinthe boma tikanyalanyaza mawa tizalira

 23. What you are saying you people are the expectations,don’t forgat the more you expect the more you get disappointed.hope what you are saying are you predictions but you can’t undergo each and every malawians’ mind,beware of it.if you want to say,say which is rated to you not speaking like we Malawians have sent you to do so.speak in your own behalf ok?.keep the date I have said this and you remind me after 2019 elections if DPP will loss the elections….focus,focus,focus..wait wake..you will tell.

 24. If Mcp is a changed party why it’s log is still black cock? Why allowing crooked policians like Mia? remember, is one of the circled politicians. Which party doesn’t he joined? We want a serious new party with new faces. Peter honourably should give a chance new blood also to govern this country

 25. Yes you will win becoz if you say no confidence, peter will just fire u.
  Dausi hopefully u understand how corrupted is your party.

  Even a one year child knows you are lost in all.

 26. I can see thousands of people who are going to explode in 2019 when they will hear that we take over again this is DPP time and with will continue KKKKK u already know friends

 27. Dausi shud just wait and see..we are the ones who casts votes..just as they have done in by elections,DPP will also lose the 2019 elections with a land slide…a Malawi anatopa ndikunamizidwa…confesion with no actions is useless ..DPP no moreeeeeeee

 28. atazakuvoteren ndindan mmene mutizuziramu mot mukuona ngat ndfe opusa muzaziona muzalira ndithu m c p itengaso boma ndpo tili pambuyo pawo a dpp musazivute ai

 29. How is this going to be mr ……… Or are you having another malawi somewhere? Because rationale and truly speaking, people you hava had on by_election, very same people are the ones you are going have on the mega elections

 30. koma daus wakulad mesa amauza athu kuti Ku sanje awina nanga bwanji sanawine lelo akuti 2019 awina bwanjiso amalakhula bodza bas ndipo iyeo anali wodulisa ma card mu MCP so nawo a piter akumusungulichan aonenga chipan cha DPP akanachoka amenewa a manabas 2019 sakuwina awa onse azabwela mu MCP chipana chao chakale blv me

 31. Akati “should not be cheated” watipanga cheat ndani a MEC????????? Koma iwowo ndiamene apangidwa “cheated” chifukwa amanyengeka ndi kuchuluka kwa anthu mmisonkhano saziwa kuti anthu amatha kuchuluka ngakhale pa ndeu ya ana.

 32. Kumeneko mkulira Adausi mzako wakumenya wakuchotsa mano mkumangoti ndibwezela koma ukumuona akupita potelopo nde kuopako vomelani Adausi

 33. Mbava ya Maize Gate sadaichotse paudindo m’chipanimo mpakana pano, Maphunziro a ku Secondary adachotsa mayeso a JCE, Mitengo yogulitsira mbewu ndiyotsika momvetsa chisoni pamene mlimi akufuna kugulanso zipangizo za ulimi kuchokera ku zokolora za chaka chatha, kuchedwa kulandira malipiro kwa ma Civil Servant, katangale mma department onse a boma, kuzimazima kwa magetsi; kungotchulako zochepa zedi, kodi munthu wanzeru n’kutenga vote yake kuupatsa mtundu umenewu???

 34. Dpp is a failed party. All what they do is putting money in their pockets at the expense of poor malawians. Am angry with people of Mayani. Why did they even consider voting for this useless party. So upset. 2019 we must vote them out at all cost mwatienjeza.

 35. dausi wa misala iwe palibe zowinanso apa zanu zathaa tatopa ndi za chinyengo kwanu kwathaa basi kaweteni mbuzi kumudzi

 36. Kodi u president WO uzingokhalabe Ku Thyolo mukuganiza a Malawi ndi opusa inu a Dausi mukunamatu amalawi asegula maso tsopano . a China Muthalika anavala mask kumaso pano yabooka tadziwa kuti ndi Mbala izi ,zinathawa mzikomuno milandu nthawi ya kamudzu kamudzu atamwalira ndikubweranso kumatibera. Nthawi yakwana tsopano kuti a Malawi ayankhule chilungamo. Tatopa nanu anthu okuba inu.

 37. Malawians are tired with foreign leaders , MCP is a mother party that built Malawi why should we not bring it back in the Government . We need a matured party not playful parties like DPP full of crooks .

 38. The Dpp People Are Untrue Malawian Coz The Real Malawian To Day Are Crying Coz Of Foolish Govt So How Do Think They Going To Win?Izi Ndiye Mbava Zenizen Zosagailana Ndalama Komanso Anthu Aku Dedza Mayani Anthu Ovetsa Chison Kobasi Mwina Ndalama Zidabedwa Zinja Adapatsa Anthu Amenewa

 39. You’ve forgotten your dull professor will be 79 years by 2019, mark my words campaign ivutilapo, those who are very soon ditching dpp will heavily decampain this devil dpp, just wait, mass resignation is offing. Even Dausiyo akomoka

 40. adzavote nda amalawi osati a DPP ndimanyazi chabe anthu pano adaona sithawi ya bakili yot anthu adali andwiiii kkkkkk tatopa ndi mabodza komaso kuxuza amalawi ngat DPP ndidziko pamene ndi chipani choti tsikulina mudzatsika muntengo mulimo

 41. You have wrong mathematics DPP.you told us you are wining by land slide. But you have lost by land slide. Now you say 2019 you Will win.can’t you c the wrong maths again? Black cock, is coming in slow ly, aaaaa mpaka nsanje tambala wakuda. Now it will be thyolo. Kkkkkk

 42. The more you talk like that Dausi the more people become wiser to kick you.Laying is the things of cheap politics
  5-0
  Its not 5-1
  Mphungu ndi conselor zosafanana

 43. Kanamizanani kubomako mungowapusitsa bwanawo.Ngati mulikuba first term kubwanji yomaliza.Nkhanza zanuzo mulupangira kampen ena {MCP}Idzawina ngati mukukaika khalani odikira.Tatopa nanu umphawi palibe chiktwkoma ai.

 44. Kkkkkkkk who told you DPP to win 2019? I hope you expected to win these you have lost. I have seen here DPP has wrong mathematics. People in Malawi has lost hope with this government.the right Mathematics can prove themselves we have seen here. Unless kuba DPP can do.kkkkkk. zoona nsanje LA LA nje black cock. Dziko libweleranso Ku nkaka ndi uchi.

 45. Tiyeni guys tiwasapote MCP mwina mkubweletsako chitukuko. timachita manyazi ife tikamayenda maiko azathuwa kutiseka kuti Malawi idzatukuka liti,number3 pa dziko lonse lapasi kusauka choncho ndani angatipatse ulemu koyendaku? banja lopanda chitukuko linadzichotsa ulemu kamba kokhalira kupemphetsa, chonde tiyeni tigwirane manja pothandiza a MCP kulowa mu boma tidzasangalala tikazangotero.Awo akutitenga ngati ana awo,akopolo awo, zitsiru zawo asiyeni tikumana 2019 ino

 46. Dausi iwee usapusise anthu kodi iwee unari kuti 1994 usamangosutse ndizopanda pake zomwe ufune usafune 2019 tambala akudya chimanga kodi chimanga chingadye chingadye tambala? ??kapena tambala kudya chimanga samara Dausi ndpakamwa pako

 47. A Dausi kudziwa kuyankhula sikutanthauza kuti muli ndi mzeru ndi tizizungu tabodzato kumakhala kubitsa utsiru mukanakhala wamzeru mukanangoti “ayi tisintha tikonza molakwikwa” simple not “eeee we have loose the battle we have not loose the war!” Asa kumavomeleza

 48. DPP always win while pple sleep.Remember what happened when UDF officials handed over a Presidential leadership 2 unknown person and afterwards tinabeledwa zisankho zomwe mpaka pano sitikudziwa chinsisi chake.Now,ngat zipani zitatu:UDF,PP ndi MCP sizigwirizana chimodzi (kupeza kaberedwe kachisankho) DPP will be there pokapokha mutapanga mapemphero monga munachitira kwa late professar atakumangilirani pa mtengo uku akuthelani chitedze(mabvuto).

 49. We have a long way to go b4 the 2019 elections. DPP has got enough time to correct its mistakes and win again electrorates’favour. As for the MCP,Malawians hopes are on it. Therefore it must avoid complacency. Victory is not gain on a silver platter.

 50. Kumbukiran Kut 2014 Mumati Dpp Singalowetso Boma Koma Munakhumudwa Ndiye Ngat Munthu Wakulu Watero Khulupiliran Ndithu Mufune Musafune Dpp 2019 Bomaaaaa!!

 51. CHIDZIWITSO KWA AMALAWI NONSE

  Chifukwa chamwano , mtopola , munyodzo , komaso ufiti umene mwapanga amalawi povotela chipani cha *MCP*kutiyalutsa ife a *DPP* munya kuyambila mawa no Magetsi ndi madzi , agalu inu , anthu osayamika , zoona tinayetsesa the past two weeks kukupatsani Magetsi mwakathithi koma lelo kutikana chonchi , mbuzi inu.

 52. If it will be Malawians voting then MCP Will win but if it will be Dausi and his team then they will win the elections. The writing is on the wall that Malawians are tired of the sufferings from this regime. Let them be daydreaming they will wakeup in 2019 after voting when people of Malawi will have spoken through the ballot as they have just done in these by elections

 53. Keep fooling yourselves…ife pheeeeee kumangokuyang.anani mukututumuka ngati finye….ikakwana nthawiyo tizakuphwesanisoni ngati pa ma by elections….simunkateloso ma by elections asanachitike

 54. mcp cant win in 2019.impossible. if mcp think this is a litmus test of it winning in 2019 then you are cheating yourself but this election will invigorate the dpp party and the democratic forces of Malawi to join hands and prevent the autocratic mcp from nearing sanjika palace and capital hill.and this election has angered the dpp voters who took it simple not to cast their vote.come 2019 massively dpp will have its full numbers in the south and take its quarter share in the central to win.who wins in the populated thyolo mulanje phalombe chirazulo zomba and blantyre wins the elections.dpp will win no doubt.check Dedza now.

  • malawians berong to different parties and the party with the majority wins the election. ngati pali chowawa kwa dpp is the loss in nsanje otherwise lilongwe south east imayenera kuwina mcp.same ku nathenje kwa gwengwe but does not mean that automatically dpp will lose in 2019.no.remember its the incumbent party in government and expect deliberate programs which will woo voters to vote for it.subsidizing fertilizer as low as two thousand kwacha.money for work.poaching heavyweights in all districts. development projects.even money hand outs of which nobody can match. billions. dpp cant lose in a typical Malawi

  • @ ndhlovu am a nyau hardliner.mbunde yeni yeni koma za mcp ayi kumanzere.imachulutsa zopweteka anthu.its policies and ideologies.like kwawo mkwao programes.nde iwe waku muhuju uli phee kutsatira congress.blind following.kumvetsa chisonie

  • Kodi ngati ndalamazo sanagawe kuno tazidyatu mwina sukuziwa Koma sitinawavotere, nthawi nthawi yotengeka ndi zimenezo inapita ife tikufuna mfundo zothandiza anthu kuzidalira okha osati ma handout ayi. Tazidya amwene Koma aluzabe,tizadyanso azaluzanso.

  • tidzawina.nkhani ndi yokopa anthu kuti akuvotereni.dpp will woo voters. no party is a saint.you believe your party is clean ? uli kutali.politics is just dirty dirty and dirty.

  • Dada Ur Trying To Tell Us Chilungamo Koma Wachulutsa Fundo Less Uti Malawi Ili Nd Zipani Zosiyana Siyana Wakunamiza Ndani Tulo Silabwino Moti Wekha Sunaone Kut Zipani Zatsala Ziwili Basi Hahaha A Dpp Osamabisala Kumbuyo Kwa Udf Mwana Ongoyamba Dazi Akupusitsani Pilizi Musapuse Tidakakhala Kuti Ma Phone Athuwa Ku Charger Pa Solar Satheka Sibwezi Iwe Nd Ine Tikulemba Ma Comnt Ngat Tsoka Iro Azimaso Eti Kkk…, Koma Dppppp,,,,

  • inuyo mwasithika chan ndi dpp kuchoka 2004 ija osamavotera chibale koma good leader ship, alepera kutenga mazi pa salima to Lilongwe kuzipatla makwala kulibe, magets koma misokho dairy mra ma vat akutolera each and every shop Malawi muno koma osauka azirirapaka liti? arahu akbru!!! arahu akbru

  • @James. dont expect what government will do for you but what you will do to your government. don’t worry your mcp will continue with free healthcare. it will stop taxation. it will end or eradicate poverty within a year.blind follower.check the party policy and ideologies. ukamaliza go to their manufesto.dpp is a necessary evil.fortunately its ruling and will rule beyond 2019

 55. thinkn vocaburary can rule malawi, its old time where malawian were interested in vocaburary/confusion, now they have reliase , that listening to vocabulary is like listen to tongues that u cnt translate(useless) …malawian no longer need word compaign from ruling but actual doing………..its gud time u should go & rest ,thanking that u forfil vision to rule, this is not blood selection(si ufumu uwu) let other rule, God will bless if u accept other to rule ,………….

 56. Dpp is wounded and is dying. It has now joined, the mighty udf aford, pp and others in the relegation zone. If much effort is not put to revive it, it will soon be history. Dpp leaders have now lost faith and will face 2019 elections ndi chikaiko. They take malawians for fools and the pple have retaliated. They have been taught some bitter lessons

 57. ndipo ife a MCP tidzamaka zedi, galimoto iliyonse tidza searcher kaya ya POLICE kaya ya MEC kaya ya MDF kaya yopanda reg number nanjinanji ya DPP, simudzaupeza mpata. vuto ndilakut ngat umachita zoyipa ndipo tsiku la tsoka likafika, Mkono wa YEHOVA umakutalikira.

 58. The problem is not you Mr Dausi but you are suffering from incomplete anticipation. Whatever your views are, these results should tell you that Malawians can not be taken for granted anymore. Tell Mr president reality of the issues if really you wish him to rule this country for another term.

 59. What do you mean ((Malawians must not be cheated!?))) Iwe Mr Bombastic #Dausi??..

  What you are telling people here is like telling stupid people kuti umabereka pomwe ulibiretu mwana anta ndi mmodzi yemwe while someone ali ndi ana atatu koma ali duuuuu.

  Osamangokonza Mavuto akudimadzima kwamagetsiwo bwanji kuti mwina musadzachotsedwe ndi dzikwanje!??

  Iwe Dausi suukuwona apa kuti ndichimodzimodzi mkalasi mwana akamakhodza ma terminal exams 90% zimatipatsa chilimbikitso kuti mayeso omalidza adzakhodza bwino?

  Wangosowa chonena apa eti!!!
  Pepatu ndalemba mchichewa paja sukulu udaphunzira ya #welekisi yama #Bombastic

  ****Akutanthauzira anthu****

 60. Mwayambaso mwano? Inu tangokozani zomwe mukalakwitsazo aMalawi atayananu chikhulupiliro pliz pliz DPP muzimvako zonena anthu kasamva,mwano,ndeu,chipongwe,kudzikonda,kukondelana nokhankha ndizina zambiri zonsezo muziyang’anile bwino koma mukapanda kusintha believe me or not come 2019 mudzaluza.

 61. To lose 5:1 it seems that the strong wind is blowing to the side of the loser and you must be aret atleast mukadapezako Phungu m’modzi ndi khasala mwina amalawi tikadamati bolaniko 5:1 abale game yakula iyi

 62. chonde inu A DPP samalani ndithu pano athu azindikilano ndipo sakufuna kumanamizidwa kwambiri mwava amati wakutsina mkhutu ndi mnasi nde mukuwona ngati 2019 athu sakuwona mudzalira ndithu kozani mavuto onwe amalawi akukumana nawo plz magetsi akuzima mthawi yayitali mukuti athu adzipanga bwanji maka Ntchito zoyendela magetsi

 63. Ndindani ankadziwa kuti MCP inga winner. Ku ndirande BT for the past 25 years MCP sidawineko koma relo yapezeka kuti Ku ndilande kwenikweniko yapeza cansala kuonetsekatu kuti MCP yaleroi ilibe tsankho LA dzigao panopo ikulowa paliponse so DDP be carefully paja enanu mukaluza mmangotenga nfuti nkudziombela nokhaaaa

 64. Guys DPP Nd Bomaa Bac Mufune Musafune,,peter Nd Amene Mulungu Anamuloza Or Mutawuwa Motan,muzingowuwa,wuwuuwuu,zopanda Phndu, Iye Ali Ku State House Bac,,,zamuwawa Akayanike Ufa Pachngwe,,tambala wanuyo walamula kwakwana,,.tkupta chtsogolo bac..kuopa tisanduka chulu cha mchere,,by elections skanthu,,muona 2019 Nkhondo Yake..DPP BOMAAAA,APETER WOYEEE,DAUSI WOYEEE,ND MTONDO UMENE UJA..PETER CHALA CHNAMULOZA BAC ND NTHAW YAKE..

  • Muli Mu Malawi Mo Muno?.. I Don’t Think So!, Mmene Zinthu Zilimu, Basi Busy Praising Peter Hmmm. My Ccta #Change Goal.. May B Azanthu Ndinu Amakhumucha!, Koma Choti Udziwe Ndichakuti, Ngati Iwe Ukugwiritsa Ntchito Tab Popanga Comment Apa, Mind Si Tonse Tili Ndi Ma Tab Ena Amagwiritsa Ntchito Ti Ma Itel: What I’M to say z dat, ziwani kuti azanu akuvutika chifukwa cha dpp/pitala, how?.. magetsi, mankhwala kusowa,madzi+manyi e.t.c. honestly speaking dpp inali ya bingu osati iyi, nawenso ukhoza kundivomereza!.

 65. Kodi pitalayo ndi mwana muzingo munamiza mpaka liti zithu zikuonongeka 1 pitalayo anthu samufuna Iwe dausi anthu atopa nawe ndiwe yemwe umakana zipani zambili pano ukudyelela ndiwe uganiza anthu akuva ukamati MCP yoyipa 23years MCP isakulamula mwana wabadwa kathawi kameneka ugamuze kuti MCP yoyipa ukunama Ku school ana anasiya kutenga history makono

 66. hahahaha when will these DPP morons learn? The results are a clear indication that DPP is sinking deeper and deeper and yet this brainless dausi STIll thinks he can dupe malawians. Infact based on what dausi has said more people would commit to vote to prove him wrong!! By the way why is he talking about 2019 instead of discussing the current results? that’s a clear sign of fear, feeling insecure and uncertain. This is a warning to all aspiring and practising politicians never take the electorate for granted don’t take advantage of high level of illiteracy and poverty!!! people are watching and they will painfully stab you through vote

 67. Zakaesala zipite kwakaesala zamulungu zipite mnyumba yake yamulungu no matter ungathawire kutalisi chamtundu wanji tsiku limodzi uzapezeka tsomba itakumeza ndikukakusanza komwe udachokera kumpingo

 68. Kodi munthu akavotere aGoodal Gondwe,a Chaponda ,a Henery Musa ,a Ntaba , a Dausi onse akalamba awa alibe vision ya Malawi mpariament ikangoti 10AM onse tulo mikonono umachita kuveka pa TV tikufuna achinyamata ife mwava a Dausi atisungire Malawiyu

 69. Mine is just an advice to the MCP if DPP win the coming election I hope u will be decent enough to accept defeat like what the DPP has done .

 70. I like the way Dausi has said we will plan…. the issue is not campaign but give a Malawians what they want not what you are loading at them. They need this load to be taken upon them. The now and then famine, jobless, moneyless, poor health, merit etc. Promises and lies. ETC. The time is now

 71. Dausi is the one who make’s peter to loss 5-1.munthu oyipa uyu and ndimunthu m’modzi akuchititsa kt peter asakondedwe ndi amalawi.akumamuuza zabodza m’tsogoleri zotsatira zake akumaona ngat zinthu ziri bwino.KODI MKAZI UKAMUKANIKA KUCHIPINDA(ndirande malabada) NDE KU BAFA UKAMUKWANITSA?

  • no way!! bwampini himself is a stupid baboon! he has studied and seen how his fellow DPP scavengers behave why can’t he guide and set standards? he the toothless bwampini himself is the most stupid creature!!

 72. I agree with Alex….Its us Malawians that are going to vote n 2019 and not you Mr Dausi,that’s just a sign that DPP gonna lose the coming election….Mufune musafune koma DPP pa MCP sizadusa and that’s gonna be the down fall of the party

  • Ukunama ase apapa ndipamene mwatipatsa mangolomela , ndipo ife achainuwake DPP ndipamene tigwilane manja kuti 2019 tidzateteze ilamulilo wa DPP

  • Muyambe kaye mwasiya zikwanje tikufuna Malawi saving bank yathu muwuze mulankho wa lomwe ubweze ndalama za NEC bwampini apepese mafumu aku mpoto athu aja mudampha pamwambo wa tumbuka.

  • @ J Sedo…..Are you a foreigner or a Malawian?,,,,remember in Malawi we go for majority.If Malawians r supporting MCP az you have seen 5-1,who are you to say u gonna unite az DPP members kt muzawine?…gone is that time and let’s give chance to other parties 2 take over….Be wise my friend and remember what Calr Boston n 1870 said,”tolk wisely to avoid people measuring your stupidness “

 73. Mr man u mustconsult the doctor now b4 thngz becom worse, it seems that CEREBERUM or Medula mwainu mulibe.

  Zindkilan mmela mpoyamba, vomelezan kutuluka mboma timasiilana iz.
  U’re saying u’ll win in 2019 yet u’re failng today so who will vote 4 u mr mp? Ee3ee answer’tu!!!

  • Sir Blessing tchuzi kaye pang’ono, bwanawotu pamene adangotuluka ku MCP mu 2006 sadawinekoso masankho ya Phungu wa kunyumba yamalamulo anthu akwawo adawadziwa kuti ndi adyera chisoni chabe chomwe likuwachitila boma lawolo la DPP pomawapatsako timaudindo monga ukudziwa kuti undindo waunduna ulingati m’mene Yesu Amkasankhira Ophunzira ake sionse ophunzira ake amene adawapeza msunagoge ena amkawapeza ku nyanja akuwedza nsomba ndichifukwa chakeso kuno nduna zathu zimathaso zili kunja kwanyumba yamalamulo ndiye mbale wanga ukalankhura kuti bwana Mp ndithu ndithu mwanna ukhala ngati ukuwachitila mwano anthu akumwanza chifukwa ukuwapatsa mp amene sadamufune, amene adamuzindikila kuti tsiku lina adzawaonongera zinthu, ndatha ndine mbale wako ndimangokukumbutsako izi

 74. Mr. Dausi,why can’t u accept the defeat,ur speeches are always negative,ndinu amene mumayipitsa dpp,go home muzikalima nandolo mwakalamba,kudya ndalama zaulele

 75. Zopopa magazi zake zimenezi mabesa ma vote inu bas kma makan mukuona ngat anthu sakuziwa kut mwatengapo mbari pa nkhan yopopa magaziyi

 76. Sitimafuna kuyakhira Dausi,is dreaming usapangitse abwanako Bp ikwere kwanu olo kubera zimakuvutani tione ngati adzavote abanja
  Lako

 77. Dausi Dausi si iwe unapusitsa angwazi lero ukufuni umupusitsenso pitala koma Dausi kodi iwe mmesa upisitsa chakwamba kuti ayambitse chipani Dausi bodza lidza kupha

 78. Dissapointment can be a great motivator in some scenarios and small wins can sometimes distruct ones goals….all i can say is both sides need to be alert, or both are going to be ambushed. The future is always unpredictable.

 79. Inu DPP izawina 2019 khulupilirani.Monse momwe Dpp sinawinemo,mkuyambira kalelonse madera amenewo Dpp imavutika.Palibe angatenge u Pulesidenti ameneyi asanamalize materm ake.Belive me.

 80. Komatu ma electricity blackouts anyanya ndiye mavotiti akuluzika apa ……strategise for 2019 but know that the worst enemy of DPP is Escom

 81. Ine poyamba ndimangofuna kukumbutsa Gulu lonse limene limadzitcha kuti ndila dpp choti mudziwe ndichakuti mtengo wautari sulila chikwangwani, ndipo dzuwa salozelana, ndalankhula izi maka pogwiltsa ntchito zichewa zomwe Adausi angathe kumva bwino, zachitikazi likhale chenjezo osatinso phunzilo chifukwa likakhala phunzilo mutha kukonza zolakwikazo, ndipo ndikunena monenetsa kuti pamene mukukonxekela kuchoka m,boma please tayesani kuchepetsa kuwanamiza anthu, ndipo muziesetsa kunenako chilungamo. Osamangothamangila kuwanyoza amene akukudzudzulani ayi. Apa anthu akudziwani kuti pamoyo wanu chomwe mumadziwa ndikutukwana ndikukolezela ziwawa kudzela mwama youth Cadet anu nde samalani. Za 2019 iyo ndinkhani ina amene angazafike kumeneko ndamene axaone xomwe zitazachitike. Musakhale ndichizolowezi chomati ayi tizawina amene akavotewo mukuwadziwa kuti azakavotela inuyo? Nanga apapa chakuvutani ndichani kuti asakuvoteleni? Ndiye mudziwe kuti amalawi si Ana anu kuti muzingowazunza ali ndiufulunso osankha xomwe akufuna. Inuyo yanu nthawi yatha ndipo vomelezanu kuti Amalawi akufuna kuona zina.

 82. afrobarometer idatichenjeza,mudawatukwana.Lero atibabada mukuzizilitsa.Muzatiluzitsatu inu a dausi ndi jeffrey.Kasaila ndiye akukwanitsa ntchito

 83. Malawi wapenya zomwe Dpp inapanga pp pa chisankho cha 2014 panopa Dpp iziona 2019 apa yangomba Dpp kuona zokhoma Mcp yangolawitsa chabe 5~1 zizindikilo zoti Dpp kwinako izizatuluka ndi zero..amalawitu awona kuti boma ili limasaukitsa anthu osauka kale limalemeletsa anthu olemera kale kumaziikila kumbuyo kuti silakuba pomwe ndilimene limaba boma ili silifuna kuveka ndinkhani zakuba limazitchinjiliza…koma amalawi kumangosauka boma ngati la pp linaveka ndikuba koma zinthu zimayenda koma iziiii za Dpp akuti siziba koma olo chimod choyendako boma lose akuti wakuba ndi chaponda

 84. Khalidwe la umfaka mpweya…
  MCP woyeeeee

  2019 adzavota ndindani? Mesa ndi ife tomwe.. nde mukumangowina pa kamwa bwanji? Hahaha

 85. NDILEMBE DZADZIKULU KUTI OWELENGA MUDZIWELENGELE BWINO. MCP SIINGAWINE 2019 AI. ALIYESE ZIMENEZO ADZIWE CHITAKHALA CHIPANI CHINA BOLA KOMA OSATI MCP.

  • IWE PACHIMTUMBO PAKO WAMVA INE SINDINABADWE LELO NDINABADWA NTHAWI YA MCP ZAKA 4 MCP ITATENGA DZIKO KWA AZUNGU. NYANSI ZA MCP NDIMAZIDZIWA UNGANDIUZE CHIYANI PATHAKO PAKO WAMVA UDZINGONGA COMENT KOMA NA ZOTUKWANA ZOKHAZO NDIYE KUCHINTUMBO KWAKO PACHIBWISI. MCP NDIYOTSUTSA BASI KULIBWINO KULAMULA CHIPANI CHINA OSATI MCP.

  • Kikikiki amene amachita nyasi mu mcp ukuwadziwa bwino panopa chipani chomwe ali ukuchidziwa bwino.tisalimbane nawe. chakwera,msungama,sitolo kunalibeko mu mcp imazunza anthuyo. umufunse dausi akuwadziwa azinzake omwe amazuza nawo anthu

 86. Mnamizeni pitalayo ife a Dausi tili pa ground pompo ,DPP siingawine anthu akulira. Pali zambiri zoti mukonze. Lero ma services onse a boma palibe chaulele. Katangale wakwera pafupifupi 100 percent. Ma driver kumakhomera ma laisensi awiri .mphekesela zikumveka mma chalichi mukhale msonkho, ndiye a Dausi mukamalankhula mitima ya anthu ikumakwelanso

 87. Mwayamba kuwanamiza APM abwana musawamvere akufuna kuti muzitulusa ndi kuwapasa ndithu akunama awa.MCP Yakalipa sizocheza maka kuno kumwera ndi kubvuma pambuyo pa Mia

 88. Who is going to vote mr Dausi to say you ll win in 2019??? I think ur brain is not in good shape and its like all of us belong to dpp shame on you and keep on dreaming!! Kulota salesana.

 89. kkkkkk kma boma ili kaya mwina kma na ine, ineyo…
  ndikulumbila cheke cheke thwaaaa sindizayelekeza kuvotela boma..
  lokupha anzathu achi alubinoli, la anamapopali, lobela chimanga pa nsaluli, lomangoyatsatsa magetsiliii
  achinyamata ndikumangofila pheni lol.

 90. Dausi you are a disgrace indeed you and your fellow crooks have totally cheated Muntharika, the Nsanje lalanje election has proved this. As long as you, your wife and children vote in 2019 DPP will win, but if Malawians vote, you will face the exit door. Sometimes I wonder why such DPP is showing such arrogance as if there is a mechanisim that puts them into government apart from voting by the Malawian themselves. WATCH OUT!!! THE CLOCK IS TICKING

 91. Who is going to vote? Dausi or citizens? We have just send a massage 2 days ago DPP 1 MCP 6 still you have a gut to tell us you victory? That was a warning shot. #2019CHAKWERA inde tavomera

 92. paja ma by elections amaneñanso chimodzi modzitu… we have no reason to believe him..akuopa kuchotsedwa ñtchito nde aķanama bodza lomwelo kwa munthalika choliñga adye nawo ndalama źa boma mpaka 2019. palibe cha nzeru angakambe ķuti tingamukhulupilire..