Andipase lipoti la ndalama za Covid apo bi! ndisumila DODMA, watero Idriss Ali Nassah
M’modzi mwa anthu olankhulapo pa momwe zinthu zikuyendela mdziko lino a Idriss Ali Nasah wati asumila nthambi ya boma yowona ngozi zogwa mwadzidzidzi ngati silipeleka lipoti lofotokoza bwinobwino momwe ndalama za boma zokwana K6.2 biliyoni… ...