Mwana wafa ku Machinga atadya nsima ya gaga
Mwana wa zaka zisanu ndi ziwiri wafa pomwe wina akulandira thandizo la mankhwala pa chipatala cha Machinga atadya nsima yomwe anaphikira gaga m'mudzi wa Makangata. Mwana yemwe wamwalirayo dzina lake ndi Yamikani Witness wa m’mudzi… ...