Makolo ena ku Thyolo ataya mwana chifukwa cha umphawi
Makolo ena ataya mwana wa mwezi umodzi pa chipatala chachikulu cha Thyolo, ponena kuti sakwanitsa kumusamala. M'neneri wa apolisi m'bomali, Sergeant Rabecca Kashoti wati m'mawawu, munthu wina anapeza mwanayo akulira kwambiri pamalo oimitsira njinga zamoto… ...