Apolisi ena adandaulidwa ku Mzimba kuti akugwirizana ndi akuba
Pakati pa mwezi wa June ndi July, 2024 anthu m'boma la Mzimba anavutika kwambiri ndi anthu akuba mowopseza pomwe anthu ena ochita malonda adavulazidwa. Ndipo anthu awiri akugwira ukaidi kamba kopezeka olakwa pa milandu ya… ...