Chiwelengero cha opezeka ndi Corona chafika pa 70
Chiwelengero cha anthu omwe apezeka ndikachilombo ka Corona komwe kakumayambitsa matenda a COVID-19 chafika pa 70 tsopano ku Malawi. Watsimikiza za nkhaniyi ndi nduna ya zaumoyo m'dziko muno a Jappie Mhango omwe amayankhula lamulungu pa… ...