Azanyengo ati kugwa mvula ya mphamvu kuyambira lachitatu likudzali
Pamene madera amchigawo chapakati komanso kumwera kwa dziko lino kuli nga'mba, tsopano nthambi yoona za nyengo ndi kusintha kwa nyengo yati kuyambira lachitatu pa 13 December, a Malawi ayembekezere kulandira mvula ya mphamvu. Malingana ndi… ...