Matako, ndi ena awiri, awapeza olakwa
Bwalo la Senior Resident Magistrate Joshua Nkhono, ku Balaka lapeza olakwa a Lilian Matako komanso a Ishmael Chitete pa mlandu ovulaza munthu. Anthu atatuwa akuwaimba mlandu ovulaza mwana wa zaka 9, Mercy Magombo, yemwenso ndi… ...