
CCAP Nkhoma Synod yakana mapemphero omwe anachitika kwa a Mutharika
…Synod ikufufuza abusa ake... Synod ya Nkhoma ya mpingo wa Church of Central Africa Presbyterian (CCAP), yati mwa abusa onse 53 omwe anapita kunyumba ya mtsogoleri wakale Peter Mutharika, m'boma la Mangochi kukachita mapemphero, abusa… ...