Ndikufuna kukumana ndi Chakwera – watero Winiko
Amene akutsogolera zionetsero zosagwirizana ndi kukwera kwa mitengo ya zinthu Bon 'Winiko' Kalindo wanenetsa kuti akufuna akumane ndi mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera. Kalindo amene adalepherana kumvana ndi nduna zaboma pamkumano omwe anali nawo… ...