
Tilandileni tafikanso, Blue Eagles yabweleranso mu TNM Super League
Itatuluka mu ligi m'chaka cha 2023, timu ya apolisi ya Blue Eagles tsopano yabweleranso mu ligi yayikulu ya mdziko muno ya TNM Super League kutsatira kukhala akatswiri mu chikho cha Chipiku Stores Central Region Football… ...