Blantyre Water Board ikufuna kukwezaso mtengo wa madzi chaka cha mawa
Anthu okhala mu mzinda wa Blantyre ayembekezere kuti chaka cha mawa mtengo wa madzi utha kukweraso kaamba koti bungwe logulitsa madzi la Blantyre Water Board (BWB) lati likufuna kupempha boma kuti likwezeso mtengo wa madziwu… ...