Boma alipempha kuti lichite changu popeleka zipangizo za ulimi
Phungu wa nyumba ya malamulo wa dera lapakati mu mzinda wa Lilongwe Alfred Jiya wapempha boma kuti lichite machawi popeleka zipangizo za ulimi zotsika mitengo kwa anthu okhala m'madera amatawuni ponena kuti nawo ali ndi… ...