
Abusa a CCAP Nkhoma Synod apempheleranso Mutharika
Patangodutsa masiku ochepa abusa a Church of Central Africa Presbyterian (CCAP) Blantyre Synod atayendera mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika kenako ndi kuyitanidwa kuti apalamula, nawo abusa oposa 50 a Nkhoma Synod ayendera… ...