Dan Lu watokosola aMalawi ndi nyimbo yotukwana
Anthu mdziko muno makamaka mmasamba a nchezo akulavulira zakukhosi chiyamba kale pamaimbidwe, Dan Lufani kaamba ka nyimbo yake yatsopano yomwe oyimbayu wagwiritsa ntchito mawu olaura. Munyimboyi yomwe anthu akugawana mmasamba a nchezo yomwe mutu wake… ...