Bola Chilima: Callista Mutharika ati alamu ake Peter asayimenso 2019
Waika mutu wake pa njanji mkazi wa Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Callista Mutharika. Wangochita za Yobu 13:13, kutayila uko ubale wake ndi Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika. Iwo ati kwa iwo… ...