Tikutumiza chimanga chochepa dala pofuna kuteteza ku mbava – Sam Kawale
Nduna yowona za malimidwe a Sam Kawale ati boma likhala likupitiliza kutumiza chimanga chimene likusunga mu nkhokwe zake ku misika ya ADMARC m'dziko muno ngakhale anthu pakali pano ayamba kukolola chimanga m'minda yawo madela ena.… ...