Anthu akukonda Chakwera panthawi yokhayo apatsidwa maudindo
Wa pampando wa chipani cha Malawi Congress (MCP) mchigawo chapakati a Patrick Zebron Chilondola ati anthu ambiri akulemekeza mtsogoleri wa dziko lino akapatsidwa udindo koma akalandidwa udindowo mpamene amanyoza mtsogoleri wa dziko. Poyankhula pa Mtengowanthenga… ...