Munakondwa ndi Kondwani? Kwabwela Dalitso ku DPP
Akupitadi adad kutula pansi udindo mu chipani cha DPP, koma sikuti udindo amusiyila chabe Kondwani Nankhumwa uja wakhala akuchititsa misonkhano ngati mwini wachipani. Kuli mpikisano tsopano pamene mkulu wakale wa banki yaikulu mu dziko muno… ...