Mtalimanja atule pansi udindo – Zipani zotsutsa
Zipani zotsutsa boma m’dziko muno zati mayi Annabel Mtalimanja atule pansi udindo wawo ngati mkulu wa Malawi Electoral Commission (MEC) kaamba koti alephera kugwira bwino ntchito. Zipanizi zidanena izi pa msokhano wa atolankhani omwe zipani… ...