
Anjatidwa kamba kopezeka ndi mfuti
Bambo wa zaka 42, James Kaipa, ali mchitokosi cha apolisi ku Balaka pomuganizira kuti anapezeka ndi mfuti popanda chilolezo. M'neneri wa apolisi m'bomali, Inspector Gladson M'bumpha, wati Kaipa adagwidwa ndi apolisi m'dera la Phalula pamodzi… ...