![MHRC Massah](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/07/MHRC-Boniface-Massah-235x176.webp)
MHRC yapeza a polisi olakwa pa imfa ya mwana ku Mzimba
Bungwe lowona za ufulu wa anthu la Malawi Human Rights Commission (MHRC) lati makolo a mwana wa sabata zisanu ndi ziwiri yemwe anamwalira pa chipikisheni cha Mtambalika (road block) m’boma la Mzimba mwezi wa June… ...