Matako, anthu enanso awiri agonabe m’chitokosi cha Police
Bwalo la Senior Resident Magistrate Joshua Nkhono ku Balaka lakana kupeleka belo kwa mayi Lilian Matako, a Zuberi Chitete komanso a Ishmael Chitete. Anthuwa akuwaganizira kuti adachita zinthu zofuna kuvulaza munthu. Powonekera ku bwalo la… ...