Apezeka olakwa, chigamuro pa 3 September
Anthu awiri omwe bwalo la milandu ku Mzimba lidawapeza olakwa pa mlandu wakuba moopseza akuyembekezeka kudzalandira chigamulo mwezi wa mawa pa 3 September 2024. Devie Harry adapezeka olakwa pamilandu yonse inayi pomwe Lukas Golosi adapezeka… ...