Gulitsani zimenezi – a bwalo agangalama, ati nyumba ya Mphwiyo ipitebe pa msika basi
Ngati mumakhala mukufunafuna mwayi wa nyumba ku Area 43 anaimba Tay Grin kuja ndiye sunthirani pafupi. Ndi kutheka mayankho anu muwapeza pano. A bwalo ati nyumba ya a Paul Mphwiyo ilandidwe ndithu. Oweruza milandu wa… ...