FAM isefa ma bwalo osewelera mpira chaka chino, Blantyre yatsala ndi bwalo limodzi
Bugwe loyang'anira masewera a mpira wa myendo muno m'malawi la Football Association of Malawi(FAM) lasefa ma bwalo osewerera mpira wa super league chaka chino. Bungweli lomwe lalamulanso kuti bwalo la zamasewera lalikulu la Kamuzu ku… ...