Pavuta pa msika: Shuga wasowa
Zativutanso! A Malawi ali pakalikiliki kuthamangila ku ma okala kuti apeze nawo mwayi ogula shuga yemwe akusowa zedi mdziko muno. Shuga wasala ochepa zedi mu magolosale aakulu ngati Shoprite, Peoples, Sana Cash and Carry komanso… ...