
Ku mpingo wa Mibawa CCAP omwe uli pansi pa sinodi ya Blantyre kunabuka nkangano mpingowu utakana kuyimbila maliro a membala wake ponena kuti amamwa mowa. Malingana ndi lipoti ya MBC, abale a munthu omwalirayo komanso… ...