Ebrahim Raisi
Tsogoleri wa dziko la Iran, Ebrahim Raisi wamwalira pa ngozi ya Ndege ya mtundu wa helicopter yomwe inanyamula mtsogoleriyu ndi nduna yoona za maiko ena ya dzikolo, Hossein Amirabdollahian. Malinga ndi malipoti omwe  wailesi ya… ...