Dziko la Iran lataya tsogoleri wake

Advertisement
Ebrahim Raisi

Tsogoleri wa dziko la Iran, Ebrahim Raisi wamwalira pa ngozi ya Ndege ya mtundu wa helicopter yomwe inanyamula mtsogoleriyu ndi nduna yoona za maiko ena ya dzikolo, Hossein Amirabdollahian.

Malinga ndi malipoti omwe  wailesi ya BBC yaulutsa, ndegeyi inagwa ku mpoto kwa dzikolo kamba ka chifunga.

Ndegeyo ndi imodzi mwa ndege zitatu zomwe zinali pa mdipiti pomwe a Raisi amachokera kumalire adzikolo ndi dziko la Azerbaijan.

Advertisement

One Comment

Leave a Comment

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.