Three Malawian youths who went to Israel to work in farms have been deported to Malawi after they ran away from their farms to seek employment elsewhere. This is according to Lions Recruitment Agency director… ...
Articles By Mphatso Khutcha Richard
Mtsogoleri wa mbali yotsutsa boma wa DPP kunja kwa nyumba ya malamulo a Mary Navicha, ati atengela ku nyumba ya malamulo nkhani yokhudza kalembela wa voti kuti akawunikenso lamulo logwiritsa ntchito chiphaso cha unzika poponya… ...
Yemwe wangosankhidwa kumene kukhala mtsogoleri wa aphungu otsutsa boma wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) m'nyumba yamalamulo, mayi Mary Navicha akana kulankhulapo m'nyumbayi pa zomwe mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera analankhula pomwe amatsekulira mkumano wa… ...
Mcdolnad Nginde' Mtetemela has put pen to paper as head coach for newly promoted Super League side Creck Sporting Club. Creck Sporting Club, formerly Kawinga FC, have confirmed the appointment. The coach will be assisted… ...
Dziko la Malawi pamodzi ndi mayiko ena onse padziko lapansi lachiwiri pa 13 Febuluwale limakumbukira nawo tsiku la "Condom'' pamene akatswiri ati a Malawi ambiri sakutha kupeza mwayi wa makondomu mwachangu. M'modzi mwa katswili owona… ...
Atatsanzika Mark Harrison, timu ya mpira wa miyendo ya Mighty Mukuru Wanderers tsopano yalemba mphunzitsi watsopano ophunzitsa osewera mu timuyi yemwenso anaphunzitsapo timu ya Nyasa Big Bullets Nsanzurwimo Ramadhan yemwe kwawo ndi ku Burundi. Malingana… ...
Lilongwe based giants Silver Strikers have made their third signing ahead of the 2024 season, roping in Dedza Dynamos forward Charles Chipala. Chipala on 13th February completed his move to the Area 47 based team… ...