Bambo wa zaka 24 zakubadwa adapezeka atamwalira m’nyumba mwake m’mawa wa la Mulungu mu tauni ya Limbe ku Blantyre. Potsimikiza za nkhaniyi, wachiwiri kwa m’neneri wa polisi Ku Limbe Widson Nhlane anauza wolemba nkhani wathu… ...