Former Chairperson of the Malawi Electoral Commission Jane Ansah has confirmed that she will be seeking office as a Parliamentarian. She will be gunning for a newly created Ntcheu North West seat. However, contrary to… ...
Articles By Lindiwe Sambalikagwa
Pena ngati upemphe kwa a neba kuti mwina angotibwerekako wawo, ife tiwapatse wathu. Chifukwa zimene likuchita dziko la Tanzania ndiye eee ndi zodabwitsa. Patangopita masiku pa makina a intaneti dzikoli litadya wani ndi sitima za… ...
Ngati mumakhala mukufunafuna mwayi wa nyumba ku Area 43 anaimba Tay Grin kuja ndiye sunthirani pafupi. Ndi kutheka mayankho anu muwapeza pano. A bwalo ati nyumba ya a Paul Mphwiyo ilandidwe ndithu. Oweruza milandu wa… ...
Komatu kulibe kupuma ku ma bwalo. Ili mkamwakamwa ya Dorothy Shonga osumira Mayi Easter Gondwe, a Joshua Chisa Mbele nawo awopseza kuti akamang'ala ku bwalo kuti a Gerald Kampanikiza akuwayipitsira mbiri. Malingana ndi zimene alemba… ...
Kulitu nkhani ku bwalo uku. A Easter Gondwe omwe amatchuka ndi kukamba nkhani pa tsamba lino la Facebook akasumilidwa. Doro wa Zeze ndiye wakamang'ala kuti a Gondwe ndi a 'hater' ndipo amamudyola kwabasi. Akufuna abwalo… ...
Koma zilikotu. Ati chifukwa china mabanja sakulimba, kaya anthu kumangothibulana, ndi chifukwa choti anakhadzulirana nkhuku pa chinkhoswe. Watero mwini mpingo wa Fountain of Victory, a Joseph Ziba. Mu kanema amene wawanda tsopano, a Ziba amene… ...
Amafuna kutulukira pawindo koma abwalo akamumbwandira. Mulandu wake wa katangale upitilira basi, ndipo akapezeka olakwa Batatawala n'kutheka akasewenza jele. Oganiziridwa pa milandu ingapo ya katangale, a Abdul Karim Batatawala achoka ndi nkhope ya manyazi ku… ...