The High Court in Lilongwe has jailed contractor Godfrey Dzanjalimodzi to eight years for theft and money laundering K338million in connection with the cashgate scandal. He had deposited into WG Construction, a company he co-owned,… ...
Articles By Kondwani Mkhalipi-Manyungwa
Pamene zokambilana za aphungu ku nyumba ya malamulo zangoyambapo, mtsogoleri wa zipani zotsutsa a Lazarus Chakwera anena kuti iwo ndi anzawo ayambapo kunyanyala zokambilanazo. Malinga ndi a Chakwera amenenso ali mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha… ...
Wakalamba wafuna. Mstogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika amene akhale ndi zaka 81 pofika 2019 ati iwo ndi kamnyamata kachisodzela ndipo azapikisana nawo pa chisankho mu 2019. A Mutharika anena izi mu mzinda wa… ...
A cyberwar has ensued between Malawians and Zambians over comments that the former made on a viral photo that shows the Mayor of the Capital City of Zambia, Lusaka, taking a nap at a public… ...
Inu amene muli pafupi ndi Mtsogoleri otsutsa a Lazarus Chakwera, ati muchite machawi kuwamanga zingwe ndi kumapita nawo ku chipatala cha anthu a misala ku Zomba. Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika anena kuti… ...
Amwela chikho chimodzi tsopano pa uwiri wawo, oyimba Phungu Joseph Nkasa ndi munthu wa Mulungu Shepherd Bushiri. Pamene oyimba Joseph Nkasa watulutsa nyimbo yotonza chipani chotsutsa cha Kongeresi uku akutamandila chipani cholamula cha DPP, naye… ...
Fourteen young Malawians have left the country for South Africa where they are expected to obtain skills and experience in leadership in their various fields. The fourteen will participate in a month long YALI RLC… ...