A Chakwera ndi a mpwesa, akufunika apite ku Mento – watelo Mutharika

Advertisement
Peter Mutharika

Inu amene muli pafupi ndi Mtsogoleri otsutsa a Lazarus Chakwera, ati muchite machawi kuwamanga zingwe ndi kumapita nawo ku chipatala cha anthu a misala ku Zomba.

Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika anena kuti a Bambo Chakwera amene amatsogoleranso chipani chotsutsa cha Malawi Congress akufunika akaunikidwe mmutu ndi madotolo odziwa za matenda a misala.

Peter Mutharika
Mutharika: A Chakwera ayamba matenda olondola dzuwa.

A Mutharika amanena izi poyankha Bambo Chakwera amene anawanyogodola iwo kuti ndi kathyali psipsiti, mkulu wamabodza mwina ngati dyabulosi amene.

“Ati ine ndi wamabodza,” anatelo a Mutharika pa mwambo wa Ijitima wa asilamu. “Dikilani ndikuuzeni munthu wamabodza. Munthu wamabodza amanama za maphunziro ake.”

A Mutharika ndiye anafotokoza kuti a Chakwera sakamba za chilungamo pa maphunziro awo.

Iwo kenako adaonjezelapo kuti a Chakwera atha kukhala kuti ayamba matenda olondola dzuwa ndipo akufunika kukapimidwa ubongo.

“Ndipo akuyankhula a Chakwera zingokhala ngati zoduka mutu, amenewatu mwina ali ndi misala, atengeleni ku chipatala cha anthu amisala akawapime,” anatelo a Mutharika.

A Mutharika ndi a Chakwera ayambapo kuthilana nkhoko pamene zikuoneka kuti zokonzekela chisankho cha 2019 chayandika.

A Malawi ena adzudzula atsogoleri awiriwa pa makhalidwe awo achibwana olimbana ndi kusinthana mawu ngati ana pamchenga.

 

Advertisement

260 Comments

 1. Munthu wa nzelu akazuzulidwa ndi anthu atatu amayenela kukhala pansi nkuona vuto lake apo ayi amazimangilila basi nkhutukunve

 2. Kusowa chonena ,pogwira zinthu zikamavuta umaona ngati anthu akudana nawe kenako kumaona aliyese openga ngati pali munthu mtsogolere opengetsetsa pa onse atilamulira muno ndithu ndi ameneyu akupengetsa azakeyu achibale ake kumangoyang anila mwina akudikila ayambe kutola zitsipe ndi pamene apange kanthu,dzana timalangizidwa kuti nkhondo ya mau sitithandiza pano ndi uyu akupengetsa anthu

 3. kkkk Kwa ineyo ndimaona kuti onse Peter,Chakwel,ndi anzawo wonse ndiwopenga misala,chonde anzathu inu muli kufupi nawo mupite nawo ku mentol.Chisankho tisanayambe.

 4. malawi walero azitsogoleri nthito kumangonyozana bola voti munawavotera iwo zikulowa ovotanu mufundo zachitukuko zija pano akukupangilani ntchito zonyozana .ndale sizinthu anthuwo ntchito zawo ndizimodzi

 5. NGATI CHAKWERA AKUFUNIKA KU MENTAL NDEKUTI IYE AKUFUNIKA ZIMA INJECTION ASIYE KUTIBWEBWETERA IFE…..TATOPA NDIKUMVA MAWU OTI TIYAMBA/TICHITA POMPANO…MPAKA LITI?? ZINTHU ZIKUONONGEKAZI NDIFUMBI……TIZIWONA MAGETSI 4HRS M’BANDA KUCHA,TATOPA

 6. Do you consider those wwho can’t read your language on your page? hw do we read now? even the world wats 2 learn and appreciate what goes on in your country,

 7. basi kalowen kumentoko. ine zisandikhuze.after a Chakwera then a Peter nao akalowe salibwino ndithu. enafe tizikupezan komko m’mbuyomo kkkkkkkkkkkkkkk

 8. Boma la DPP lawononga ziko.Sindikuziwa kuti pa za pezeka boma lonyasa ngati la DPP.Ndiulemu chabe anthu amuziko kunena kuti ndiwe musogolere.

 9. Munthuu akufuna atwinanso ndpo iyi ndi nkhndo akumenya.ndpo sangalore kt aluze ich nchfukwa chake iye akuipisa anthu ena

 10. ndiinu a chitsilu a president mmalo molimbana ndi mavuto mukuyambitsawa mu kuyankhula zopusa zopanda phindu Ku dziko

 11. Adzavotele dpp ndi mbuli zolima Nandolo, people who dnt know even to write the word, blind loyalty and its meaning. Tonse timadziwa kumene kumakhala mbuli zimenezi and there remote areas.

 12. Bwanji osasutsa mfundo zomwe Chakwera wa nena ndikungoyamba kutukwana Chakwera.Sadziwa Debate ena ndiitane ana a std.5 yakale awauze kuti timkatani:its better to be a nurse than a teacher because a nurse wears a white uniform
  Its not good to be a nurse because nurses touch corpses which is a healthy risk as one can easily contract diseases.Thank you the chief proposer and the chief Opposer……..

 13. ALIYENSE NDIWAMISALA ZIMANGOSIYA % YAMISALAYO MUZIYANG’ANE KAYE MUWONA PAMENE PAKUYAMBIRA MISALA YANU. KODI ZAYAMBIKA ZOMAIMA PACHULU KUMANGO LALATA. UDZA APOLICE KUTI AMUGWIRE OSATI IFE AMENE TISALI AMISALA

 14. Chakwera akuynerad kupita ku metal akufuna atiuze kut inchocho ndichomwe chili ndizeru kuposa peter kungoti ndiwe osusa panga zot magesi asamazime kuchoka pa udolo wako utatero mages osazima kusithj zithu man mavote ose azakhala ako koma man yesesan chitapon kanthu musamangosusa zinthu zopanda pake aise wayeneradi kupita ku metal akakupime mwina uzisusa za mzeru ndale wayamba liti iwe sungawine yesu sakondwa nawe posiya kutumikira wangobakoso ku mpingoko kape iwe obera nkhosa za ambuye

 15. Day’s passed, day after desolate day and she was utterly alone.Hatred and Resentment built up inside her and she could hardly go near her mother.She had been standing in the rain for more than five decades,hoping she could see a light at the end of a tunnel but to no avail. Malawi is one of the privileged countries in Sub-saharan African and perhaps the best and most affordable recreational centre in Southern Africa. Its amusing nature and stunningly amazing geographical position, rich in cultural norms and friendly people ultimately makes the warm heart of Africa an attractive place for tourists.Though its political,economic and social landscape is marred by greedy,malicious and desperados politicians.Many argue that economically, politically and socially Malawi has the most comprehensive, well thought out and cohensive plans on how to run the affairs of the country.But what leaves many in suspence is why up-to-date the economy of Malawi is still in shambles despite its well thought out plans? I mean, why Malawi as a nation has tremendously failed to boost up its economy? Why are we wasting our time formulating and reformulating various sophisticated stragies and putting forward new useless measures instead of just implementing the already existing strategic plans that are gathering dust? I never got it! Let me backtrack alittle bit. Long long time ago, Harnghzou G20 summit made a number of recommendations in which it featured some significantly incredible tips on how to make Africa Great.I read the article written and shared by Li Yang with great interest. During this summit Harngzhou emphasized the need for support for Agriculture and Agribusiness development, and the importance of broadening ,deepening and updating local knowledge base.The summit also went on outlining the significance of concentrating on green technology and investing in energy and mining industry; and focusing on new industrial revolution. And this made me think deeply about home. Now ,after reading the recommendations made by Harngzhou G20 with soberness, one can easily get it, that it does not require Sherphard Bushiri to challenge the government that he can deal with these problems in 48 hours.We already have capacity an

  1. bambo noel katete zisiyeni zangwazi ziwirizo palibe wabwino pamene paja kumbali ya nkhanza ngwazi yachiwiriyo imkafuna kupha amalawi onse pakamodzi atasunga ndalama kunyumba kwake mankhwala kusowelatu nthawi yomweyo mafuta agalimoto kusowa zakudya kukwera mtengo inali imfa imene ija bambo katete kkkkkk

  2. Chimwemwe ndiwe wabodza panopa zimene wakambazo zupezeka nanga athu 20 tsiku limdzi ndi kamuzu angovomelezani zani agogowa zithu zawavuta

 16. Chakwera moto kuti buuuuuuuuuuuuuuuuuuuuu…………..am with u

 17. Wamisala anaona nkhondo, koma ndie tonse tikhala amisalatu mdziko muno, chakwela wamisala, Wandale wamisala, ndiye wabwino m’ndani? Kapena iwo amene?

 18. Kkkkkkkk.Naneso2 Ndimaganiza Kut Iyi Simisala Muthu Wadzelu Sangathawe Tchito Yamulungu Kuthamangila Za Ziko Lapansi.Bac Mupelekele Akayambe Kumwa Raaaa!!!

 19. Chakwela vote yanga ikudikila iwe Basi enawa andilephela…chomwe akuziwa ndikupange ndalama moti apange magetsi akuti ayi koma tipange ndalama..zazziii

 20. Mukadzangowona wamisala akunena anthu amene ali mentally fine kuti ndi wopenga (if s/he is lacking some sense of reality tht s/he z not mentally stable), mudzangodziwiratu kuti misala ya munthu ameneyo ili in incurable state ndipo sasowekeranso kupititsidwa ku Bwaila(when in central region) or ST John of God(wen in North) but straight ku Zomba mental Hospa and prognosis z most of the times poor in tht state, endless kakakakaka

 21. Wamisala ndi amend akukanika kuchotsa mbabva zake ziri m’bomazo. Ubwinowake wamisalayo anaona nkhondo ndipo anthu anathawa angakale iyeyo

 22. Sindikudabwa kwenikweni bcz munthu ukamamuloza mzako zalazina umaziloza wekha ndiye apa a Munthalika muyiwara kuti zala zina mukuziloza nokha openga ndinuyo mwachidure

 23. zoonadi wamisala amaona anthu ngati a misala Kulibe dziko ndinamvapo akunena zoti chiphaso cha unzika chitha mphamvu expire date boma malawi simisala imeneyi chimene mkuyenera kudziwa a malawi si openga

 24. munati a wandale apite ku mental in within two weeks time mukutinso a chakwela apitenso ku mental. mainly who is mentally disturbed among you three? izi zi kuchitika chifukwa chosavetsetsana.

 25. muthalika yikumuwawa 5-1 dziwa izi 2019 mcp boma kulibe kubela mavoti dyelatu ndalama zabomazo ndiwe mbuzi

 26. hahahahah if chakwela is mentally in mind why akanena zithu dziko lose limagwedezeka ngat chivomelez wake up malawi let’s have change

 27. MCP ikuyenda bwino kwambili pansi pa Chakwera. Mwezi watha womwewu tawina ma MP 3 a nyuwani achinyamata okhaokha. Ma khansala 2 achinyamata. MCP 5 – DPP 1. 2019 kuli ku sesa.

 28. Amuthalika ali ndi ziwanda zosaneneka ,zoona anganyozemunthu pa zochitika za chipembedzo,pakufunika kuwapempherela ndithu mkuwachotsa ziwanda ndithu,,
  Mu ulamulilo wa peter from 2014 apanga k2000 pano akupanga k5000 three years zokha nanga atati alamulile ten years adzapanga one milliom, zikuwavuta akuluwa sadziwa kuyendetsa dziko

 29. Are those words really coming from a state president? Keep calm and be smart my president. Don’t lose temper as somebody who wants to go to mental hospital

 30. Why ku Mental?Otsutsa akati apite patsogolo ndi ntchito yawo podzudzula zaphada zanuzo m’malo mwa ife omwe tilibe”good platform”basi alakwanso?Why can’t u jst check where u actualy went wrong & make abit ‘f collections or else accept that u’v failed to lead us?Muziona zaulendo wuno,kkkkkkkkkkkkk

 31. Misala Ya Pitala Akufa Nayo Posachedwapa Coz Ndichiwewe,imagine Wandale Wamisala Chakwera Wamisala iiiiiiiiii Kungodziwiratu Kuti Wamkulu Mimbayu Ndiye Wamisala{aka Pathological Lier)

 32. Why ku Mental?Otsutsa akati apite patsogolo ndi ntchito yawo podzudzula zaphada zanuzo m’malo mwa ife omwe tilibe”good platform”basi alakwanso?Why can’t u jst check where u actualy went wrong & make abit ‘f collections or else accept that u’v failed to lead us?Muziona zaulendo wuno,kkkkkkkkkkkkk

 33. Nthawi zina tiziyesesa zochita zathu zizitha kumasiyana ndimmene tionekela,sibwino kuipa maonekedwe ndizochitazathu zimene.Palibe mzeru kutukwana Pulesidenti.apatu ndikochekera kumene mumasowa khalidwe.Yes tikuziwa kuti zolakwika,tiyeni tikambe zimenezo,osati kutukwana.

 34. Misala Ya Pitala Akufa Nayo Posachedwapa Coz Ndichiwewe,imagine Wandale Wamisala Chakwera Wamisala iiiiiiiiii Kungodziwiratu Kuti Wamkulu Mimbayu Ndiye Wamisala{aka Pathological Lier)

 35. CHAKWERA IS FAILING TO BRING UNITY IN HIS PARTY. WHAT MORE A COUNTRY, CAN HE MANAGE TO CONTROL OUR BELOVED COUNTRY MALAWI? I DOUGHT

  1. What more unity do u want chipani chawina ma byelections pompano bcoz pple worked tirelessly together as one. Which party is disunited btwn dpp and mcp here.

  2. jack up my friend. This is by election not national elections. Its just some parts of malawi where mcp is settled. Come on 2019 elections you will agree that dpp is a powerful party in malawi

  3. zoona zimenezo ampeketula chakwera sangalamulire dziko ndiponso sangawine dziko ndilalikulu ili angafunenso tambala wakuda ndi ndani

  4. I have seen thy comments, koma adzavotele dpp ndi mbuli za athu . People who dont know even how to write the word, blind loyalty, and its meaning. Mbuli zolima Nandolo. Mbuli mdziko muno tonse timazidziwa komwe zimachokera.

  5. kodi inu mco yo yawina mipando yonse musatinyansepo apa kwagweleni uko come 2019 muzaimbanso nyimbo yanuixa yoti atibela atibela kuchokela 1994 mpaka pano muzakhumudwa muona

  6. NKulira uko a Davis Mpeketula….limban mtima ndithu coz 2019 mudzalira chikhakhali…..dpp siidzawinanso basi,zavuta kuchipani akulu…a Malawi anazindikila nowadayz…ndale zopereka ndalama zinatha kalekale..olo atadzapereka dzigayo zaulele monga anachitila masiku apitawa,ai ndithu. Zavuta basi,..limbani mtima ndithu bwana Mpeketula

 36. Koma chikuchitika ndichani atsogoleri kumangolozana chala m’malo mugwirizana zachitukuko mukupanga 5pin mukut chimecho ndie chitukuko?

 37. POMPANO IFE A DPP TIYATSA MAGETSI 24/7 TIONE ANYAPAPI INU CAMPAIGN MUNENA CHANI POTI IFE CHITUKUKO MUKUCHIONA IPSANI MTIMA NDIPO MUPSADI MTIMA IFE TIUDYA UKAPSA MPAKA 2024 TIKULAMURABE

  1. Nde wati Profet Yoswa mpaka 2024?? Afikako amene uja? Akumayenda atavala chi thewela yu. Khazikhazi nyamakazi admit ku USA. Hhehehe….ife Nsanje yonse ndi Chikwawa vote ndiya MCP ndi Dr. Laz Chakwera. Nkhalambazi zakanika.

  2. Muzakhumudwa chipani chanu pano chili pa low. Chaluza zisankho pompano musachepetse kuluza mwaluzaku. Anthu pano tinapenya no more dpp after 2019

 38. kwa ineyo ndikuona ngati a munthalika ndi omwe akufunika kuchipatala cha mental Ku zomba zifukwa zake nazi: A munthalika sakubweretsa poyera umboni wa ma pepala omwe achakwera anatulutsa oonetsa umboni wa argument yawo pamene amunthalika akungoyankhula pamenepo Iwo ndamene Ali a misala. 2 chilowereni m’boma 2014 tikatenga manifesto ya DPP only 20% of it has been achieved but look here only 1 year remained to genera elections the rest is miyala ya maziko …pazifukwa zochepa ndanenazi munthu uyu akuonetsa kuperewera kwa ubongo in short wires are disconnected in his head so need a medical review especially from psychiatrist

 39. KODI CHAKWERA CHOMWE ADZAPANGE MCHANI ASANDINYANSEPO APA? MUNTHU OLEPHERA KUYENDETSA CHIPANI DZIKO NDAKAIKAA NGATI ANGADZAKWANITSE

  1. Mcp yawina ma by elections pompano iwe nkumati chakwera akulephera kuyendetsa chipani. Mutu wako ukugwira koma. Pakati pa peter mutharika wanuyo ndi chakwera olephera ndani pamenepa.

  2. MCP ikuyenda bwino kwambili pansi pa Chakwera. Mwezi watha womwewu tawina ma MP 3 a nyuwani achinyamata okhaokha. Ma khansala 2 achinyamata. MCP 5 – DPP 1. 2019 kuli ku sesa.

  3. Inu Malo omwe mwawina ma by-election anuwo mufufuze ndi ma strong hold a MCP okhaokha kukakhala Ku ndirande NDE ukudziwa low turn out anakabvota a MCP okhaokha dikirani muone ndithu

 40. Muthalikayo Pa nyini Pa Make.Mumuuze Kuti Watitopetsa Ndipo Ikanakhara Kut Ndi Mbeu Bwenzi Titangokazinga Kut IsazamelensoOnce Again Pa Chi Nyini Cha Masten AkeChonde Mundifikizile Uthenga Wangau

  1. Wamisala Ndi Pitala Akufunika Ku Mental Mwasanga Popeza Chaka Chatha Wapanga 2000 Chaka Chino Akuti 5000 Kwacha Pamenepa Wamisala Ndani Misala Ima Posa Apa

  2. 5000 sindalama ibwere tidzizayigwilitsila ntchito,mumafuna kukhale ma K50 basi?olo itatuluka K100,000 palibe vuto ndindalama bac

  3. Maclean Chidzeka Charity Pankomera Precious Evalistus Gratia Winnie Kaziputa Pemphero Samu Bridget Chiepa Vincent Soka Soka Denis Gwaza Alfred Nsona Mkhutabasa

  4. Maclean Chidzeka Charity Pankomera Precious Evalistus Gratia Winnie Kaziputa Pemphero Samu Bridget Chiepa Vincent Soka Soka Denis Gwaza Alfred Nsona Mkhutabasa

 41. Wampewesa ndiwe zaka zochepa zomwezi mpakana Kwacha ukufuna upange one million imodzi ngati kuzimbabwe ukufuna dziko lithepo chifukwa choiti iweyo wakalamba

 42. kodi inu a manyuzi, cholinga chanu chimakhala chani mukamalemba zowawitsa mitimi ya ena chonchi? mumasangalala ma sapotawo akayamba kunyoza mtsogoleri?

 43. Last week was Vincent Wandale who was mentally ill now this week is Dr Chakwera mentally disabled again kkkkkk who is next……..loading kkk aliyense otsutsa boma apita ku mental ndithu chaka chake ndi chino

  1. Amuope chakwera kuti watani amalawi simuchedwa kuiwala sure, Chakwera yemweyo muzamtembenukiranso kuyendetsa boma sizamwanatu

  2. #Ian u have a point and that is true, only that pali zinthu zina zake zoti utha kukwanitsa kuzilongosola ngakhale iweyo mkumayenda koma this gvt is failing.

  3. Dpp total failure and disgrace .Dpp inali ya Bingu osati agogowa.kulamulira ziko zawakanika. Peterayo ndiye apite kumento coz alibe clue yoti angasinthe zinthu

  4. Pepani azanga ndithandizeni ufa watha magetsi kwathu kuno anazima dzana.Zavuta akuluakulu last yr K2000,this yr K5000 next yrK10000 pitara ameneyo aliphe akuti sakudwala….

  5. kkkkk we are indeed being ruled by a mentally ill reader.. pajatu wamisala amaziona ngat iyeyo nd wabwinobwino and the rest normal people nd amisala… kkkk ndakomoka nd phwete ine ..

  6. Ndiye mukundiuza kut 7000 tidzitenga ndalama ziwili bas 5000 and 2000 peter yo waganiza bwanj peter apite Ku mentoooo bas,,, shemu

 44. galu kwabasi ayambe iyeyo kupita Ku mental coz mutu wake sugwira ai munthu chaka chatha wapanga 2000 kwacha lero akut 5000 kwacha chisilu kwabasi wandinyasa kwambili pitala

 45. Zikugwirizana bwanji misala ndi maphinziro a Chakwera? Zopanda nzeru ndipo wamisalatu adawona nkhondo nanga ma generatorwo alikuti? Wobodza ndani pamenepa

Comments are closed.