Mnyamata wina wa zaka 18 mu boma la Chikwawa amunjata atapha mzake ati polimbilana mkazi oyendayenda. Malinga ndi mneneri wa a Polisi mu bomali a Foster Benjamin, ati upanduwu udachitika pachinayi pamene abambo awiri amamwa… ...
Articles By Kondwani Mkhalipi-Manyungwa
Inu otsutsa, valani zilimbe chifukwa zoti mutenga boma 2019 ndiye ndi zosatheka, malinga ndi kafukufuku. Bungwe lina lochita za kafukufuku lati a Peter Mutharika ndi chipani chawo cha DPP akuoneka kuti ndiwo angawine chisankho cha… ...
Bwalo lalikulu la Milandu tsopano lamasula khonsolo ya mzinda wa Blantyre kuti ndi yololedwa kugwetsa nyumba zonse zomwe zamangidwa mu phiri. Khonsolo ya mu mzinda wa Blantyre inauza anthu onse omanga nyumba mu phiri kuti… ...
Zina ukamva kamba anga mwala ndithu. Pamene okuba mbuzi akutsekeledwa zaka, okuba galimoto akuchoka ku Khoti akusekelela. Bwalo la majisitileti ku Blantyre lagamula amuna awiri amene anaba galimoto kuti atsatsekeledwe. Ati m'malo mwake asachimwenso basi.… ...
Legendary musician and jazz trumpeter Hugh Masekela has died after a long battle with prostate cancer. He was 78. https://twitter.com/hughmasekela/status/955713727088775168 In a statement, his family said he had "passed peacefully" in Johannesburg "after a protracted… ...
Inatchuka nkhani yoti Wapolisi wa zachitetezo ananjatwa kamba kopita ku chimbudzi ku nyumba ya nduna zoona zophunzitsa anthu. Malinga ndi malipoti amene amagawidwa mma Facebook ndi WhatsApp, ati Wapolisi amene amapeleka chitetezo ku nyumba ya… ...
2019 sali pafupi kwenikweni koma ndale zija ndiye zafikapo basi. Pamene chipani chotsutsa cha Kongeresi chili pa kalikiliki otolela anthu, nawo a chipani cholamula cha DPP ayambapo kutsegula makomo awo. Dzulo lamulungu chipani cholamulachi chalandila… ...