2019 a Mutharika awinanso – kafukufuku

Advertisement

Inu otsutsa, valani zilimbe chifukwa zoti mutenga boma 2019 ndiye ndi zosatheka, malinga ndi kafukufuku.

Bungwe lina lochita za kafukufuku lati a Peter Mutharika ndi chipani chawo cha DPP akuoneka kuti ndiwo angawine chisankho cha 2019.

Mutharika
Kafukufuku wati a Mutharika adzawina chisankho cha 2019.

Malinga ndi bungweli lomwe lili ku Mangalande, a Mutharika adzathidzimula a Chakwera pa chisankho chaka chamawa chomwechi ngakhale a Chakwera ndi chipani chawo aonetsa kuti akuphukila.

A bungweli ati ngakhale ku Malawi kuno kukuoneka kuti chuma chikuvuta koma a Mutharika atha kuzapambanabe kamba koti chipani chawo ndi chotchuka maka Kum’mwera.

“A Mutharika ali pa chi ntchito choyenela kulondoleza chuma cha Malawi. Koma ngakhale zili choncho, iwo ali ndi kuthekela kopambana kamba koti chipani chawo chili ndi chikoka pakati pa anthu a Kum’mwera omwe ndi ochuluka,” atelo a kafukufuku.

Iwo aonjezelanso kuti kugawikana komwe kuli mu chipani chachikulu chotsutsa cha Kongeresi kukuonjezela mwayi kwa a Mutharika opambana.

Kafukufuku wa bungweli amene wachitika chaka chomwe chino wati a Mutharika sikuti azachita kopambana ndi mavoti ambiri.

Koma polankhula ndi Malawi24, katswiri pa ndale a Wonder Mkhutche anati 2019 ili kutali kuti opambana zisankho adziwike.

“Ndi ndale izi, zambiri zitha kuchitika mu nyengo iyi. 2019 ili kutali kwambiri,” anatelo a Mkhutche.

Advertisement

215 Comments

 1. point of correction
  Dr chakwera sanachotse munthu ku mcp,ife ndi amene tachotsa agwape amenewa,atoleni amenewa ku dpp paja mumakonda kutola zomwe anzanu ataya

 2. Ndikuona Tsogolo Loti Mcp Kudzawina Koma Anthu Kuzuzika Kwambili Chifukwa Chanjala Komanso Kususuka Kwatsogoleri A mcp Ndipo Amalawi Tilingalile Mozama Zosankha Mtsogole 2019.

 3. Kkkkkkk a!!!!!!!! anthu kulimbana ayi koma uwu, ena ayi koma uyu, i nvani izi Mulungu ndiamene akudziwa za munthu odzatilamula basi.

 4. Am an ordinary Thyolo citizen…no any kind of this shithole research conducted so far…brainwashed liars…Malawians now are no longer of that acient times akudya phalabungus.Zibwebwetani.Tizaona.

 5. Mutharika sangaluze zisankho za 2019 pangabvute maka,ngati anawina 2014 from opposition,,, ndie what more pano akulamulira

 6. Opusa ndi omwe azavotere DPP yo….a Malawi tatiyeni tizikhala ozindikira posankha Mtsogoleri.Taona mavuto a DPP kwa zaka zimenezi after Peter kutenga Boma,,,ndiye mukavoterenso Peter yemweyo…???Kodi inu ngati kuvota simutha bwanji osangosiya avote ndi anzanu omwe amadziwa kuvota mwa nzeru….???

 7. Akanakhala Kuti Ndi Ma Prophet Sindikadakhulupirira Koma Ngati Apanga Mozama Kafukufukuyo,ine Ndindani?! Vuto Abale Athuwa Ali Ndi Njala Yandalama… Akuona Ngati Kulamula Dziko Ndikulemera!! Asukiratu Kale Mphika Pomwe Nyama Sanaphe!! Ali Busy Kukanganira Ulamuliro..Zikungooneseratu Kuti Atangoti Atenga Boma Azatha Kuukirana Okhaokha Komanso Kuululana Okhaokha!! Ena Ndi Aja Ayamba Kale Kufuna Zawo Atawagwiritsa Thangata Achinyamata Pomazetsa Ziwawa Nthawi Ya Ma Byelections… Mia Ndi Amzako Shame On U!

 8. Zabodza kafukufuku wachiyani kumangonena zammutu ine bwanji simudanifunseko mukumudziwa yemwe ndidzamuvotere kumangofuna kupha mitu anthu ine simungandipusitse.

 9. Nkhaniyotu ovotela dpp ali pheee, samachitatu phokoso ai. koma manyaka aziwaniwa yayaya zongodziwikilatu kuti zausavege zokha zokhatu.

 10. Ndale Masuku ano ndi Business, antu amafuna kutchuka, kapena kulemera sono, kwaine ndinazindikira mochedwa kuti ndimataya ntawi yanga pachabe, kupangila campaign zipani monga (Afford) kuchoka apo ndinalowa (DPP) mntawi ya malemu Dr, Bingu wamtalika, koma pamapeto ake umpawi umapitilira ndiyeno kuona azinzanga akusogora, ndiye ndinasiya za ndale, ndikutuluka kukafuna zincito kunja. Bola kumadalira Mlungu kumampempha, amapereka zosowa zako ntawi zonse, kudalira muntu one day uzakhumundwa, “if APM will win it’s okay to me, even if Chakwera, will win it’ll be also; okay to me because

 11. Zizaoneka mwamuna mnzako mpachulu umalinga utakwerapo ndipo linda madzi apite ndipo udziti ndadala inu akafukufuku musokoneza anthu komanso kuli bwino kungokhala osanena chili chonse chifukwa nthawi zina mumaputa mkwiyo mmitima ya wanthu chonde mungalakwitse zinthu you cannot do things 100 percent across the country. So you cannot decide on your own on this matter but people will judge the election komanso musamawaputsitse amalawi iwo wokha amadziwa chochita ndipoakudziwa

 12. Sadzawina amenewa kodi akukamba zopusazi koma akuona momwe ife amalawi tikuvutikila mdzikomuno? Zachuma, Katangale, Magetsi, kuphatikiza apo ifeakumudzi timadalira zakumundapanozinthu sizilibwino chimanga, Nandolo, zatsikantengoudyokobasi. Ndalama sizikupezeka bwino bwino mavuto okhaokha ndalama akungophangira kuti azidzapangila kampeni.

 13. Kaya azawina,Kaya azaluze, Ine ndilibe nazo ncito chifukwa ndinatopa kudalira chipani, kapena Boma ndimaziimira paine ndekha, Ndiponso ndinatuluka ku Malawi, kalekale chifukwa chosowa chisamaliro ku Banja langa, Aliyense azawine ine ndi wanga, Zokangana ndiza NDALE ndinasiya ndimapanga chitukuko pandekha

 14. MMMMM Tiyamike kumalankhula moti dzikoli ndilomodzi? Ndipo zautsogoleri zili yapo koma tatieni tingoukonda mtundu uliwonse Wa anthu not kumaoneka ngati wina ozindikila wina osazimdikila. Ukamati kanthundu kajaka iweyo ukutanthauza chani? Ndipo ukufuna akumvele ndani? Ndipo iweyo ntundu wakowo wapambana chani? Ndipo phindu lomwe umalipeza iweyo ndiphindu lanji? Panotu ndipochezelela not kukumbana mitundu, ndibwino ngati zolemba zasowa kungosiya kudzisungila ulemu, ufuna akumvere ndani iweyo? Ndipo ndale zikuthandiza chani? Uzipanga zokuti zizikuthandiza iweyo ndachibale ako zinazo zikuchedwetsa.

 15. Sometime our disires fails not kuti ifeyo sitinachite bwino koma timakhala kusemphana ndi nthawi atha kudzawina chifukwa nthawi ya awo mukuti oluzawo sinakwane zithaso kutembenuka kudzaluza chifukwa cha nthawi yomweyo kuti nthawi yawo yatha izi sindimazikhulupilila za kafukufuku amatinamiza vuto limakhala ofukulayo ali ndi mbali kale ndiye amatseka makutu kwa awo akuonetsa kusakhala mbali yake,mtima unatilimba kuli zaka zoposela 50 kuti tidzapeze mtsogoleri ofuna kutukula malawi panopa ndi game zikwanje osauka chawo palibe

 16. The platform will in addition to this page allow our readers to interact on various posts. Send the join request, our administrators will add you right away. To access on free mode: https://free.facebook.com/groups/969694746503465?refid=18&_ft_=qid.6515647752647087639%3Amf_story_key.1106750499464555%3Atop_level_post_id.1106750499464555%3Atl_objid.1106750499464555%3Apage_id.585331951512518%3Apage_insights.%7B“585331951512518”%3A%7B”role”%3A1%2C”page_id”%3A585331951512518%2C”post_context”%3A%7B”story_fbid”%3A1106750499464555%2C”publish_time”%3A1516862861%2C”story_name”%3A”EntGroupMallPostCreationStory”%2C”object_fbtype”%3A657%7D%2C”actor_id”%3A585331951512518%2C”psn”%3A”EntGroupMallPostCreationStory”%2C”sl”%3A6%2C”targets”%3A%5B%7B”page_id”%3A585331951512518%2C”actor_id”%3A585331951512518%2C”role”%3A1%2C”post_id”%3A1106750499464555%2C”share_id”%3A0%7D%5D%7D%7D&__tn__=C-R

 17. Kkkkkk koma kuli fumbi ladzaoneni yaa mulungu ndiyemwe amasakha mnsogoleri not munthu akumuziwa ndiye mwini tisapindirane mashati iiiiii gayez.

 18. Akuluakulu a MCP ali ngati agalu oti akuthamangitsa Gwape koma pamene ali pafupi kumugwira nkuyamba kulumana okhaokha.Zikutinyasa zikuchitika mu MCP zi ndipo mmalo mokakuvoterani tidzangokhala osakavotaso zomwe zidzapatse mwai ena kuti awine.We know that some officials are getting somethig to bring confusion in the party 4 it 2 luz.

 19. Chigawo chapakati ndi capital city yathu kwakwana,pankhani yausogoleriyi ndiye izichokera kumwera,nduna zikuluzikulu ndi kumpoto basi.Inu mcp yalamula zaka zingati??.Mufune musafune achigawo chapakati analamula mokwana ndipo sazalamulanso ndipo sitingalore ndipo sitizalora kuti azalamulenso zikoli.Musamaganize kuti anthu anali opusa kuchosa mcp kapena kuti ayiwala.A mcp tazilotani muzaziona.Ndikumamva chisoni kwambiri ana osapola pamchombo akunena za mcp,mukawafuse makolo wanu akakuuzani za mcp.Pano anthu mukumatha kutukwana Pulesidenti,nthawi ya mcp mufuse ngati mukanati muzinena zonyoza msogoleri,Ena akuti pano mcp ndiyasopano chabwino,MCHIFUKWA CHANI SAKUSINTHA ZINA LA CHIPANI AKUNGOTI MCP.Tazinamizani zozalowa m’boma tizaona ife ovota ndiwomwe mutazatimve ndi mkwiyo omwe pano mukutikumbusa wa mcp zomwe amkatipanga mma 70’s -80’s.

  1. Kkkkkkk koma mesa Dausi anali ku mcp? ndiye aziti mcp ndiyakhaz ndekuti Amapaga ndiyeyo pano mcp ilibwino Osamana apaKkkkkkk mcp bom!!!!!!!

 20. It is too early to make predictions but if we take the present situation, he cannot win bcoz people re angry. The issue of electricity and high cost of goods ve negative impact on his leadership style.

  1. Mr Lipenga i just wanna remind u Chakwera is also a proffessor but he uses his proffessorship on the basis related to his proffessorship dat z y ur so called president #pitara wanted to ruin proff chakwera’s image by sayin he is a fake proffessor

  2. mmmm bt umust kno 1 thing about Malawi’s politics its not easy kuchotsa chipani cholamula n MCP sidzalamulilanso Malawi kufuna osafuna Dpp ikutenganso boma 2019 ine ndinabadwila muMcp paphata penipeni paDz koma Im moving with time let the past b past events

 21. Kodi mumawatenga a Malawi ngati anthu osaganiza Peter wapanga chiyani chimene angawalodzere Amalawi? True leader anali his late brother uwu unalidi ntunda wa Malawi may his soul continue resting in peace.Magesi ndi awa akutha wk asanayakewa ngati mdziko mulibe Nsogoleri shame.Olamulira Malawi 2019 akumudziwa ndi Mulungu bc chifukwa ndi amene akudziwa mabvuto amene a Malawi akukumana nao.Every problem in lyf have an expiry date am sure God is hear our criying.

  1. Lero limenero mwayamba kumati bingu anali mtunda???…if you look at peter’s developments with an mcp eye then you wnt see his succeses..what i know God is the best judge

  2. kma ndthu ndzodandaulitsa pano ndpo mwawona kt Bingu anali wamaxo mphenya pot adafa kma ali moyo simudamuyamikile mudamuzuza ndziwonetsero alot of criticism ndzowonad chitsime chmawoneka kuya kwake chikaphwa kma chonde tiyen tisinthe tiziwayamikilalo atsogoleri athu akadalimoyo ngat atichitila zabwino osat akafa may the soul of bingu rest in peace

  3. 2019 DPP boma basi. Kongelesi should just start preparing some court papers as always. They are now oozing with confidence after winning the by elections thinking that pple will give them another chance to rule Malawi again. No way . 4ward ever , backward NEVER .

 22. The pollsters said Trump would lose, it’s how I know that these things are not always right!

  But with the lack of exceptional candidates, I may vote for him again. At least economically we are better than we were a few years ago!

  1. Man inflation is down into the single digits. Yes, beating inflation introduces some major challenges. But the economy becomes stable. Purchasing power is better than it used to be!

  2. Inflation yoputsitsa azungu a IMF. Dziko likukhalira most of the time mu blackout, lero hunger is looming ahead, fodya timadalira uja watsowanso chifukwa cha chilala. 1 digit yanuyo is just on a peace of paper, pa ground mitengo yazinthu ikunka nikwera.
   Ziputsitsani azungu amalola kuputsitsidwawo, amalawife sitikuona nawo economic stability yanuyo.

  3. Inflation yoputsitsa azungu a IMF. Dziko likukhalira most of the time mu blackout, lero hunger is looming ahead, fodya timadalira uja watsowanso chifukwa cha chilala. 1 digit yanuyo is just on a peace of paper, pa ground mitengo yazinthu ikunka nikwera.
   Ziputsitsani azungu amalola kuputsitsidwawo, amalawife sitikuona nawo economic stability yanuyo.

  4. Things are going up daily, civil servants salaries are still low, school fees in both secondaries and universities are very high whereby an ordinary malawian cannot manage, unemployment rate is very high, boma kulemba anthu ntchito idasiya kalekale. Corruption rate is also high, anthu akuba akungowasinga chipanicho osawamanga, koma nkumawayankhulitsa pa msonkhano,
   I dont think zimene ankalonjeza pa manfesto yawo zija adazitsata.
   One digit yomwe ikukambidwayo ndi zomgokomera anthu achuma kale pamene munthu wakumudzi mmmmmmm kulira daily

  5. Benson Njiwa mukunena zoona wakulu sindikukana ayi. I withdrew from college myself because I couldn’t afford it. Ndipo ndimakolo ambiri omwe sangakwanitse ma fees a masiku anowa. Ngakhale zili choncho, ineyo point yanga ndiyakut a zipani zinawa alibe ndondomwko zabwino zotukukira Malawi. If you ask Chakwera how he will reduce mavuto ngat awa I don’t think he will bring a good solution. Because anali ndi mphavu yoletsa kapena kuimika kukwezedwa kwa ma fees koma sanapangepo kanthu!… Mu parliament akuchita Chani vhopindulira iwe ndi ine otsutsawa??

  6. Everything is Spiritual my friend.
   The Bible says bad leaders shall bring calamities on their people. So to answer you yes hunger and drought are caused by DPP. Kusamvera ndi kuopa Chauta.

  7. Has MCP presented their Manifesto? NO. So how can you judge something you have not yet seen?
   Of all the advice’s MCP gave DPP, has DPP listened to any of them? NO.
   DPP yapindulira chani to the ordinary Malawian? NOTHING.
   Ndi chifukwa chake in DEMOCRACIES anthu amavotera zipani zina kuti aone maluso ena.
   Nkhalamba zalephera, full stop.

  8. Leroi Nanthambwe I have nothing against MCP and I’m not pro DPP. Advice ukunena kut anaperekayo inali yoti cha?? inform me please. Maybe I can change my mind. My intention is not to vote next year!

  9. Let’s try other leaders like Chakwera, he has a clean background in politics, maybe he can turn Malawi into a better place. This government doesn’t take advice from opposition eg MSB sale. After the sale almost 250 employees were expelled. So many corruption cases involving top officials koma akungowayang’ana, ndi zambiri

  10. Benson Njiwa Please if you have time read “the principles of micro economics”… you’ll understand that privatization is very good. However, people lose jobs but overall it frees the market. Besides, MSB was lending too much from the treasury. It was consuming too much from the treasury!

 23. peter sangazaluze coz amakondedwa kwambri ndi anthu akumudzi pamene abusa chakwera amangopopedwa pafacebook ndi ana oti sazavotanso nkomwe..DPP ndiyowina

  1. Kumamasura adzipsa mtima winayo Dpp m’boma ng’onazo ife ayi i hate mcp 4eva chifukwa adawadulitsa card mai anga alindimimba akuti mudule macard awiri nthawi imeneyo

  2. After winning the by elections , they think that they have already won the 2019 general elections. The crocodiles are still celebrating not knowing that the 2019 elections will be a different ball game.

  3. Ine ku mudzi kwathu kulibe okonda dpp ndipo mufune musafune mcp 2019 boma. Dpp iwina bwanji chi(ireni 2014 siinawinepo ma byelections.

  4. akanakhala kut anthu amavota pa facebook i would i agree wth u kut MCP izawina kma ngat mavote ake ndiomwe timapanga aja MCP palibe chawo Take it or not

  5. Synet…dont b cheated with facebook mcp supporters jonehasburge wing..they dont vote…kuyambira kale kulibe dpp mcp has been winning by-elections but come to general elections they fail..why?? The MCP name reminds them their past how youth millitias had to torture citizens

 24. Inenso ndikugwirizana nazo ngakhale boma la mutharika sindilikinda,chipani chomwe chikuoneka kuti ndichamohanvu kwambiri ndi chija cha Ku lilongwe congress paty tsono ife anthu akumwera tinapondelezedwa kwambiri ndipo pano sitingayelekeze kuika kantundu kajaka pautsogoleri wadziko

 25. He will win indeed. chifukwa all people who makes noise on Facebook are very few,of which half of those few ali ku jozi omwe samavota..Odzavota ali duuu mmamidzi ndi mmakwalalamu. Chakwera is only famous on social media which is used by mostly none voters like me. Like me,had it been am not on social media,I swear,Chakwera sindikamuziwa like wise 70% of people who are not on social medias. facebook is full of tiana ta ma under 18 who only makes noise

  1. Mmm Man Mavuto Aky Amenewa Chaka Chno Chokha Ndvota Tichose Pitarayu Chakwera To The Top Bax Ngakhaly I Dont Hv Chpan Bt Lc Ndpasa Vote Yanga

  2. 17OCTOBER TINAVOTADI PA FB NDIKUWINA 2019 CHIMODZIMODZINSO.VUTO CADET NDIMUNTHU WAMAKANI KWAMBIRI,B4 17 OCT BY-ELECTIONS KUNALI MAKANI OKHA OKHA EVEN ATALUZA KUNALI MAKANI OKHA OKHA.MUKHALA CHONCHO A DPP ANZANU AKUTHA MTUNDA!!

  3. Unless am mad may be. Voting for an 81yr old granny. Kupusa chani? Anthu okhwima mu nzeru achichepere atha ku Malawi kuno?

 26. Teti fibombe,ba peter kuteka 2019,Meleibepa,Amalawi tulo be like South Africas pple they dont fear,bagonani mukadali kuvutika.Malawi ndi dziko ling’ono koma silikutukuka kamba ka achiphazi opondereza.Ayesu bwerani msanga kuzachosa achiphaziwa atikwana

 27. Apm Adzawinadi Akunena Zoona Akafukufuku Sakunama!Mcp Mtsogoleri Wake Akanakhala Wina Tikanat Adzawina Koma Lazaro Chatsika Wamakaniyu?Ndakaika Koma Kuno Sanafike Kudzandifusa Akafukufukuwo.

 28. Dpp musamaganize zoluza ndatitu achakwela adzakhala chatsika 2019 maka adzabwelela ku utumiki ndikomwe adzakhale mtumiki weni weni wa mulungu.

  1. kkkkkkkkkkk tilolela kusiya kae castle lite kut tikasunthe mbavazi…tikatelo tizapitlize ulendo malume

 29. Kafukufuku wanena yekha…ndipo sizabodza I know wina wapsa mtima…..& akanati DPP iluza mukanati zowona hehehehe …..sinavoterepo chipani choluza ine

Comments are closed.